
Akuti aChakwera anali munthu wabwino, koma anawasokineza ndi amene anawazungulira.
Nde mufunse kuti “owazungulirawo pano anapita kuti?”
Mupenza kuti onse akanawazungulirabe, happily so. Ndipo ambiri mpakana anawaika mu shadow cabinet yawo.
Nde what’s the message? Isn’t that a warning for us never to dare him again?
Ine nde olo mvula itamagwa kuchoka pansi kupita kumwamba, I can never vote again for an indicisive slow and street-dumb person. I know what this country needs and I can’t be loyal to individuals for personal benefits more than I am loyal to the nation.
President ochita mantha ndi manyazi kuchotsa anthu osankha yekha? Never!!! And you don’t learn and change in your 70s. What you are is what you are at this age… We cannot expect anything new from a man at that age. No scientific theory supports that thinking.
Another big problem in our party is that most loyalists from central region think Malawi starts from Chatoloma and ends at Bembeke. Munthu akadzadzitsa anthu pa Mponera ndi pa Chinkhoma basi, akuti adzawinanso.
That’s why you are still waiting for Lilongwe Rural votes mpakana lero. Kuganiza mofuchilira.



