Skip to content

Malawi Cables Online

We Report the Future — the Only Trusted Source of News with a Difference

Primary Menu
  • Home
  • Latest
  • News
  • Breaking News
  • Religion
  • Economics
  • Politics
  • Sports
  • Home
  • Politics
  • KABWIRA, CHAZIYA ASEMPHANA PA GANIZO LA A CHAKWERA LAKUTI OFUNA KUIMILA MMAUDINDO AZIPELEKA NDALAMA
  • Politics
  • Religion

KABWIRA, CHAZIYA ASEMPHANA PA GANIZO LA A CHAKWERA LAKUTI OFUNA KUIMILA MMAUDINDO AZIPELEKA NDALAMA

Malawi Cables November 9, 2026 (Last updated: November 9, 2026)
IMG_8395

Phungu wa chipani cha Malawi Congress Party (MCP), a Lawrence Chaziya, adzudzula ganizo la mtsogoleri wa chipanichi, a Lazarus Chakwera, lofuna kuti anthu omwe akufuna maudindo osiyanasiyana m’chipanichi azipereka ndalama potengera udindo womwe akufuna kupikisana nawo.

Polankhula kwa Nsundwe pa mwambo wokhazikitsa mbendera womwe unakonzedwa ndi phungu wa ku Delari, a Edwin Chileka Banda, a Chaziya ati ganizo lofuna kuti munthu azipereka ndalama malinga ndi udindo womwe akufuna kupikisana nawo silikumveka ndipo sangagwilizane nalo.

Ganizoli linabwera pambuyo poti akuluakulu a MCP akambirana za momwe chipanichi chingapezere ndalama zokwana K2.5 biliyoni kuti chisankho cha mkati mwa chipani chitheke m’zigawo zonse za dziko, kuyambira ku Nsanje mpaka ku Chitipa.

Pakadali pano, otsatira MCP omwe analipo pamsonkhanowo akuyembekezera kumva maganizo a a Jessie Kabwira pa zomwe a Chaziya ananena.

Izi zikuchokera pa mfundo yakuti pa tsiku lomwe ganizo lokhudza kulipira ndalama kwa anthu ofuna maudindo linakambidwa, a Kabwira analiponso koma sananene chilichonse panthawiyo.

Ena mwa otsatirawo akufunsa ngati a Kabwira apereka maganizo awo pa nkhaniyi, makamaka poganizira kuti akuti akufuna udindo wa mlembi wamkulu wa chipanichi, womwe pakadali pano uli m’manja mwa a Richard Chimwendo Banda.

About the Author

Malawi Cables

Administrator

Malawi Cables is a dedicated news platform committed to delivering timely, accurate, and credible coverage of events and stories from Malawi and beyond. We aim to inform, educate, and engage our readers through in-depth reporting, insightful analysis, and impactful storytelling that sets us apart.

Visit Website View All Posts

Like this:

Like Loading…

Related

Post navigation

Previous: “I CAN OFFER SOLUTIONS TO THE PROBLEMS THE DPP GOVERNMENT IS FACING” – KABAMBE
Next: Former UNIMA DPP Wing President, Deputy National Youth Director Express Interest To Contest For DPP Candidature in 2030 Elections

Related Stories

IMG_8404
  • Latest
  • Politics

PRESIDENT MUTHARIKA DEFEATED CHAKWERA, BUT CAN HIS SUCCESSOR DO THE SAME?

Malawi Cables November 9, 2026
IMG_8396
  • Latest
  • Politics

Former UNIMA DPP Wing President, Deputy National Youth Director Express Interest To Contest For DPP Candidature in 2030 Elections

Malawi Cables November 9, 2026
IMG_8321
  • Latest
  • Politics

MCP Beats Ruling DPP in Mmbelwa District Council Chairmanship

Malawi Cables November 6, 2026

Recent Posts

  • MERA YASEKA MALO OMWETSERA MAFUTA AGALIMOTO A MOUNT MERU KWACHINSAPO ATI KAAMBA KOSUNGA MAFUTA OKWANA MALITA 1000 MOPANDA CHILOLEZO
  • DUWANA MUHAMMAD STARTED WELL AT MARANATHA HIGH SCHOOL ACADEMY
  • SEVEN CIVIL SOCIETY ORGANISATIONS CHALLENGE NGORA OVER DEREGISTRATION OF 36 CSOs INCLUDING HRDC
  • PRESIDENT MUTHARIKA DEFEATED CHAKWERA, BUT CAN HIS SUCCESSOR DO THE SAME?
  • Mtunthama Police OC Accused of Demanding Sex From Suspect’s Wife in Exchange for Husband’s Release

Categories

  • Breaking News
  • Economics
  • Home
  • Latest
  • News
  • Politics
  • Religion
  • Sports

You May Have Missed

1794237154036
  • Latest

MERA YASEKA MALO OMWETSERA MAFUTA AGALIMOTO A MOUNT MERU KWACHINSAPO ATI KAAMBA KOSUNGA MAFUTA OKWANA MALITA 1000 MOPANDA CHILOLEZO

Andy Ten November 9, 2026
1794234985483
  • Latest

DUWANA MUHAMMAD STARTED WELL AT MARANATHA HIGH SCHOOL ACADEMY

Andy Ten November 9, 2026
IMG-20261109-WA0139
  • Latest

SEVEN CIVIL SOCIETY ORGANISATIONS CHALLENGE NGORA OVER DEREGISTRATION OF 36 CSOs INCLUDING HRDC

Andy Ten November 9, 2026
IMG_8404
  • Latest
  • Politics

PRESIDENT MUTHARIKA DEFEATED CHAKWERA, BUT CAN HIS SUCCESSOR DO THE SAME?

Malawi Cables November 9, 2026
Copyright © 2026 All rights reserved. | ReviewNews by AF themes.
%d