Skip to content

Malawi Cables Online

We Report the Future — the Only Trusted Source of News with a Difference

Primary Menu
  • Home
  • Latest
  • News
  • Breaking News
  • Religion
  • Economics
  • Politics
  • Sports
  • Home
  • Blog
  • Home
  • Latest
  • APOLISI AMANGA MLONDA WINA KU MULANJE KAAMBA KOGWILILIRA MWANA WAZA SIZANU NDI CHIMODZI (6)
  • Latest

APOLISI AMANGA MLONDA WINA KU MULANJE KAAMBA KOGWILILIRA MWANA WAZA SIZANU NDI CHIMODZI (6)

Andy Ten October 23, 2026 (Last updated: October 23, 2026)

Pamene nkhondo yolimbana ndi nkhaza kwa Ana maka atsikana malipo akuwonetsa kuti pali ntchito yaikulu yoti igwiridwe pamene apolisi m’boma la Mulanje akusungira mchitokosi mlonda wa kampani yolima tea ya Lauderdale Tea Estate, Dalitso Majawa, pomuganizira kuti wagwililira mwana wa mkazi wazaka 6.

Malingana ndi wachiwiri kwa mkulu wofalitsankhani za apolisi ku Mulanje Joseph Topola wati mwanayo amachokera kusukulu ndipo nthawi yomwe amadutsa pafupi ndi kampaniyo mlondayo anamukokera mwanayo mu nkhalango ndikumugwililira.

Tapola wati azakhali a mwanayo ndi amene anazindikira za kugwiliridwa kwa mwanayo ndipo anakanena ku polisi zankhaniyi zimene zinapangitsa apolisi kugwira ndikumanga mkuluyo.

Majawa akuyembekezeleka kukaonekera ku bwalo la milandu posachedwapa kuti akayankhe mulandu womwe wapalamulawu

About the Author

Andy Ten

Editor

Journalist from Mangochi former student and University of Malawi, The Polytechnic

View All Posts

Like this:

Like Loading…

Related

Post navigation

Previous: INKOSI CHINDI OF MZIMBA HAS DIED IN INDIA WHERE HE WAS RECEIVING MEDICAL TREATMENT
Next: OGWIRA NTCHITO ZA ZA UMOYO WADZIPHA KU NTCHEU MWANA WAKE WAZAKA 7 AKUONA

Related Stories

IMG_7883
  • Latest

Chimwendo Banda Says MCP Is the Answer to Problems Malawi Is Facing Today, Eyes 2030 Comeback

Malawi Cables October 24, 2026
Screenshot
  • Latest

ONE EVENT, THREE DIFFERENT REPRESENTATIVES: JUSTIN SAIDI PUTS MUTHARIKA’S LEGACY AT RISK

Malawi Cables October 24, 2026
1000133738
  • Latest

FOUR MEN ARRESTED IN NKHATA BAY IN CONNECTION WITH ARSON INCIDENT THAT DESTROYED 19 HECTARES OF MACADAMIA FIELD WORTH K2.17 BILLION

Andy Ten October 24, 2026

Recent Posts

  • Chimwendo Banda Says MCP Is the Answer to Problems Malawi Is Facing Today, Eyes 2030 Comeback
  • ONE EVENT, THREE DIFFERENT REPRESENTATIVES: JUSTIN SAIDI PUTS MUTHARIKA’S LEGACY AT RISK
  • FOUR MEN ARRESTED IN NKHATA BAY IN CONNECTION WITH ARSON INCIDENT THAT DESTROYED 19 HECTARES OF MACADAMIA FIELD WORTH K2.17 BILLION
  • ONE EVENT, TWO DELEGATIONS: CONFUSION OVER WHO REPRESENTS PRESIDENT MUTHARIKA AT CCAP ANNIVERSARY
  • OGWIRA NTCHITO ZA ZA UMOYO WADZIPHA KU NTCHEU MWANA WAKE WAZAKA 7 AKUONA

Recent Comments

No comments to show.

Archives

  • October 2026
  • September 2026
  • August 2026
  • July 2026
  • June 2026
  • May 2026
  • April 2026
  • March 2026
  • February 2026
  • January 2026
  • December 2025

Categories

  • Breaking News
  • Economics
  • Home
  • Latest
  • News
  • Politics
  • Religion
  • Sports

You May Have Missed

IMG_7883
  • Latest

Chimwendo Banda Says MCP Is the Answer to Problems Malawi Is Facing Today, Eyes 2030 Comeback

Malawi Cables October 24, 2026
Screenshot
  • Latest

ONE EVENT, THREE DIFFERENT REPRESENTATIVES: JUSTIN SAIDI PUTS MUTHARIKA’S LEGACY AT RISK

Malawi Cables October 24, 2026
1000133738
  • Latest

FOUR MEN ARRESTED IN NKHATA BAY IN CONNECTION WITH ARSON INCIDENT THAT DESTROYED 19 HECTARES OF MACADAMIA FIELD WORTH K2.17 BILLION

Andy Ten October 24, 2026
Screenshot
  • Latest

ONE EVENT, TWO DELEGATIONS: CONFUSION OVER WHO REPRESENTS PRESIDENT MUTHARIKA AT CCAP ANNIVERSARY

Malawi Cables October 24, 2026
Copyright © 2026 All rights reserved. | ReviewNews by AF themes.
%d