Skip to content

Malawi Cables Online

We Report the Future — the Only Trusted Source of News with a Difference

Primary Menu
  • Home
  • Latest
  • News
  • Breaking News
  • Religion
  • Economics
  • Politics
  • Sports
  • Home
  • Blog
  • Home
  • Latest
  • RBM YATI MUNTHU ASAPEZEKE NDI NDALAMA YOPYOLA $1,000 POPANDA CHILOLEZO CHILOLEZO
  • Latest

RBM YATI MUNTHU ASAPEZEKE NDI NDALAMA YOPYOLA $1,000 POPANDA CHILOLEZO CHILOLEZO

Andy Ten September 23, 2026 (Last updated: September 23, 2026)

Reserve Bank of Malawi yomwe ndi banki yaikulu ya dziko lino yakhazikitsa lamulo latsopano lomwe likuletsa kuti munthu adzikhala ndi ndalama zakunja zopitilira $1,000 (pafupifupi K1.75 million) popanda chilolezo cha bankiyi.

Izi zili chomwecho malingana ndi lamulo lomwe linapangidwa pa 7 September ndipo analisindikiza mu buku la boma losindikiza malamulo a tsopano pa 18 September lotchedwa Foreign Exchange (Limit on Physical Possession of Foregn Currency) lomwe

Bankiyi yati aliyense otenga kapena kutumiza ndalama zakunja zoposa $1’000 kunja kwa dziko lino ayenera kukhala ndi umboni kuti ndalamazo anazigula pa msika ovomerezeka kapena akuyenera kutenga chilolezo kuchokera ku bankiyi.

Banki ya Reserve yayikanso lamulo loti ndalama za dziko lino za Kwacha zomwe zikuloledwa kutuluka m’dziko muno popanda kufunsa chilolezo ku bankiyi ndi ndalama zofanana ndi $5,000 kwa ochita malonda kunja kwa dziko lino komanso $100 kwa ena opita m’mayiko ena pa zifukwa zina.

Lamulo latsopanoli ladza imene dziko lino likukumana ndi vuto la kusowa kwa ndalama zakunja komanso kukula kwa mchitidwe ogula ndi kugulitsa ndalama zakunjazi pa msika osavomerezeka kapena kuti Black Market pachingelezi.

About the Author

Andy Ten

Editor

Journalist from Mangochi former student and University of Malawi, The Polytechnic

View All Posts

Like this:

Like Loading…

Related

Post navigation

Previous: Bambo Wa Zaka 24 Wafa Amayi Ogulitsa Matupi Atamumenya Pamalo Ogona Alendo Ku Chikwawa

Related Stories

1000106992
  • Latest

Bambo Wa Zaka 24 Wafa Amayi Ogulitsa Matupi Atamumenya Pamalo Ogona Alendo Ku Chikwawa

Andy Ten September 23, 2026
IMG_7074
  • Latest

FROM “CEMENT GATE” TO “LAND GATE”, CHUNARA IS BACK WITH MORE POWER ON LAND IN ADL, MAGWERO AND SALIMA

Malawi Cables September 23, 2026
Screenshot
  • Latest

CDEDI writes Parliament over looming drug crisis as CMST fails to pay USD18 million debt

Malawi Cables September 22, 2026

Recent Posts

  • RBM YATI MUNTHU ASAPEZEKE NDI NDALAMA YOPYOLA $1,000 POPANDA CHILOLEZO CHILOLEZO
  • Bambo Wa Zaka 24 Wafa Amayi Ogulitsa Matupi Atamumenya Pamalo Ogona Alendo Ku Chikwawa
  • FROM “CEMENT GATE” TO “LAND GATE”, CHUNARA IS BACK WITH MORE POWER ON LAND IN ADL, MAGWERO AND SALIMA
  • CDEDI writes Parliament over looming drug crisis as CMST fails to pay USD18 million debt
  • ANOTHER COURT ORDER STOPPING MEPA FROM ENFORCING USAGE OF THIN PLASTIC BAN

Recent Comments

No comments to show.

Archives

  • September 2026
  • August 2026
  • July 2026
  • June 2026
  • May 2026
  • April 2026
  • March 2026
  • February 2026
  • January 2026
  • December 2025

Categories

  • Breaking News
  • Economics
  • Home
  • Latest
  • News
  • Politics
  • Religion
  • Sports

You May Have Missed

1000107193
  • Latest

RBM YATI MUNTHU ASAPEZEKE NDI NDALAMA YOPYOLA $1,000 POPANDA CHILOLEZO CHILOLEZO

Andy Ten September 23, 2026
1000106992
  • Latest

Bambo Wa Zaka 24 Wafa Amayi Ogulitsa Matupi Atamumenya Pamalo Ogona Alendo Ku Chikwawa

Andy Ten September 23, 2026
IMG_7074
  • Latest

FROM “CEMENT GATE” TO “LAND GATE”, CHUNARA IS BACK WITH MORE POWER ON LAND IN ADL, MAGWERO AND SALIMA

Malawi Cables September 23, 2026
Screenshot
  • Latest

CDEDI writes Parliament over looming drug crisis as CMST fails to pay USD18 million debt

Malawi Cables September 22, 2026
Copyright © 2026 All rights reserved. | ReviewNews by AF themes.
%d