Skip to content

Malawi Cables Online

We Report the Future — the Only Trusted Source of News with a Difference

Primary Menu
  • Home
  • Latest
  • News
  • Breaking News
  • Religion
  • Economics
  • Politics
  • Sports
  • Home
  • Blog
  • Home
  • Latest
  • Bambo Wa Zaka 24 Wafa Amayi Ogulitsa Matupi Atamumenya Pamalo Ogona Alendo Ku Chikwawa
  • Latest

Bambo Wa Zaka 24 Wafa Amayi Ogulitsa Matupi Atamumenya Pamalo Ogona Alendo Ku Chikwawa

Andy Ten September 23, 2026 (Last updated: September 23, 2026)

Apolisi ku Chikwawa atsimikidza kuti Maxwell Nsomera wa zaka 24, wafa gulu la amai ogulitsa matupi litamumenya pambuyo pa mkangano womwe unabuka ku malo ogona alendo a Tiyamike Rest house ku Nchalo.

Wofalitsa nkhani za apolisi ku Chikwawa a Dickson Matemba ati a Nsomera lolemba lapitali nthawi ya 2 koloko m’mbandakucha akubwelera kunyumba kuchokera ku mowa analowa m’nyumba yogona alendoyi.

Matemba wati malemuwa adapeza zipinda zonse zogona alendo zili zodzaza ndi amai ogulitsa matupiwa ali ndi makasitomala awo zomwe sizinamisangalase Nsomera.

Pamenepa Nsomera anayamba kulalatira makasitomalawo zomwe sizinasangalatse amai ogulitsa matupiwa omwe anamumenya mpaka kumukomola pambuyo pokangana ndi m’modzi mwa iwo, amai enawo asanalowelere.

Matemba anati anthu akufuna kwabwino anamtengera Nsomera ku chipatala cha Montfort komwe achipatala anatsimikiza kuti wafa kamba kovulala kwambiri m’mutu.

Malinga ndi Matemba, Apolisi akusakasaka anthu omwe akuganiziridwa kuti ndi omwe achita izi ndipo akamangidwa, adzayankha mlandu wakupha.

About the Author

Andy Ten

Editor

Journalist from Mangochi former student and University of Malawi, The Polytechnic

View All Posts

Like this:

Like Loading…

Related

Post navigation

Previous: FROM “CEMENT GATE” TO “LAND GATE”, CHUNARA IS BACK WITH MORE POWER ON LAND IN ADL, MAGWERO AND SALIMA
Next: RBM YATI MUNTHU ASAPEZEKE NDI NDALAMA YOPYOLA $1,000 POPANDA CHILOLEZO CHILOLEZO

Related Stories

1000107193
  • Latest

RBM YATI MUNTHU ASAPEZEKE NDI NDALAMA YOPYOLA $1,000 POPANDA CHILOLEZO CHILOLEZO

Andy Ten September 23, 2026
IMG_7074
  • Latest

FROM “CEMENT GATE” TO “LAND GATE”, CHUNARA IS BACK WITH MORE POWER ON LAND IN ADL, MAGWERO AND SALIMA

Malawi Cables September 23, 2026
Screenshot
  • Latest

CDEDI writes Parliament over looming drug crisis as CMST fails to pay USD18 million debt

Malawi Cables September 22, 2026

Recent Posts

  • RBM YATI MUNTHU ASAPEZEKE NDI NDALAMA YOPYOLA $1,000 POPANDA CHILOLEZO CHILOLEZO
  • Bambo Wa Zaka 24 Wafa Amayi Ogulitsa Matupi Atamumenya Pamalo Ogona Alendo Ku Chikwawa
  • FROM “CEMENT GATE” TO “LAND GATE”, CHUNARA IS BACK WITH MORE POWER ON LAND IN ADL, MAGWERO AND SALIMA
  • CDEDI writes Parliament over looming drug crisis as CMST fails to pay USD18 million debt
  • ANOTHER COURT ORDER STOPPING MEPA FROM ENFORCING USAGE OF THIN PLASTIC BAN

Recent Comments

No comments to show.

Archives

  • September 2026
  • August 2026
  • July 2026
  • June 2026
  • May 2026
  • April 2026
  • March 2026
  • February 2026
  • January 2026
  • December 2025

Categories

  • Breaking News
  • Economics
  • Home
  • Latest
  • News
  • Politics
  • Religion
  • Sports

You May Have Missed

1000107193
  • Latest

RBM YATI MUNTHU ASAPEZEKE NDI NDALAMA YOPYOLA $1,000 POPANDA CHILOLEZO CHILOLEZO

Andy Ten September 23, 2026
1000106992
  • Latest

Bambo Wa Zaka 24 Wafa Amayi Ogulitsa Matupi Atamumenya Pamalo Ogona Alendo Ku Chikwawa

Andy Ten September 23, 2026
IMG_7074
  • Latest

FROM “CEMENT GATE” TO “LAND GATE”, CHUNARA IS BACK WITH MORE POWER ON LAND IN ADL, MAGWERO AND SALIMA

Malawi Cables September 23, 2026
Screenshot
  • Latest

CDEDI writes Parliament over looming drug crisis as CMST fails to pay USD18 million debt

Malawi Cables September 22, 2026
Copyright © 2026 All rights reserved. | ReviewNews by AF themes.
%d