Skip to content

Malawi Cables Online

We Report the Future — the Only Trusted Source of News with a Difference

Primary Menu
  • Home
  • Latest
  • News
  • Breaking News
  • Religion
  • Economics
  • Politics
  • Sports
  • Home
  • Blog
  • Home
  • Latest
  • APOLISI KU LILONGWE AMANGA BAMBO WAZAKA 53 PA MLANDU WOTHYOLA NDI KUFUNA KUBA ZITSULO KU KAMPANI YA CHASER CONSTRUCTION KU AREA 28
  • Latest

APOLISI KU LILONGWE AMANGA BAMBO WAZAKA 53 PA MLANDU WOTHYOLA NDI KUFUNA KUBA ZITSULO KU KAMPANI YA CHASER CONSTRUCTION KU AREA 28

Andy Ten October 5, 2026 (Last updated: October 5, 2026)

Ku Lilongwe apolisi ya Kanengo amanga a Collins Chibwana a zaka 53 woyendetsa galimoto ya 3-tonne Daihatsu nambala yake KU 700, kaamba koganiziridwa kuti anathyola Kampani ya Chaser Construction ku Area 28 pofuna kuba zitsulo.

Malingana ndi wachiwiri kwa m’neneri wa Kanengo Polisi Sub Inspector Linly Mwale apolisi amanga a Chibwana Lamulungu pa 04 September 2026.

Iwo ati malipoti akusonyeza kuti anthu anayi anafika ndima crowbars ndi zida zina zothyolera, ndipo anakwanitsa kuthyola gate ndikulowa ku Kampaniko

Sub Inspector Mwale wati anthuwa omwe analipo anayi anayamba kusanja zitsulo mu galimoto ya 3-tonne Daihatsu nambala yake KU 700.

Iye wati apolisi atafika anakwanitsa kugwira dalaivala wa galimoto yi pomwe anthu ena atatu anathawa.

Sub Inspector Linly Mwale watsindika kuti kafukufuku ali mkati kuti agwire anzawo a Chibwana omwe anathawa.

Katundu amene anthuwa ankafuna kuba ndi wa ndalama pafupifupi K10 million.

About the Author

Andy Ten

Editor

Journalist from Mangochi former student and University of Malawi, The Polytechnic

View All Posts

Like this:

Like Loading…

Related

Post navigation

Previous: TILEMBA NTCHITO APHUNZITSI 1,100 TELEMU INO- BRIGHT MSAKA
Next: MUMBA SUPPORTS EUTHINI RURAL HEALTH CENTRE WITH K4.4 MILLION ESCOM PAYMENT

Related Stories

IMG_7324
  • Latest

MUMBA SUPPORTS EUTHINI RURAL HEALTH CENTRE WITH K4.4 MILLION ESCOM PAYMENT

Malawi Cables October 5, 2026
1000115652
  • Latest

TILEMBA NTCHITO APHUNZITSI 1,100 TELEMU INO- BRIGHT MSAKA

Andy Ten October 5, 2026
IMG_7312
  • Latest

ADMARC CASHGATE: CEO BOTOLO SPENDS K40MILLION FOR ACCOMMODATION

Malawi Cables October 5, 2026

Recent Posts

  • MUMBA SUPPORTS EUTHINI RURAL HEALTH CENTRE WITH K4.4 MILLION ESCOM PAYMENT
  • APOLISI KU LILONGWE AMANGA BAMBO WAZAKA 53 PA MLANDU WOTHYOLA NDI KUFUNA KUBA ZITSULO KU KAMPANI YA CHASER CONSTRUCTION KU AREA 28
  • TILEMBA NTCHITO APHUNZITSI 1,100 TELEMU INO- BRIGHT MSAKA
  • ADMARC CASHGATE: CEO BOTOLO SPENDS K40MILLION FOR ACCOMMODATION
  • “CHEAP NSIMA CANNOT BUY FUEL ,”LEADER OF OPPOSITION BLASTS AT MUTHARIKA

Recent Comments

No comments to show.

Archives

  • October 2026
  • September 2026
  • August 2026
  • July 2026
  • June 2026
  • May 2026
  • April 2026
  • March 2026
  • February 2026
  • January 2026
  • December 2025

Categories

  • Breaking News
  • Economics
  • Home
  • Latest
  • News
  • Politics
  • Religion
  • Sports

You May Have Missed

IMG_7324
  • Latest

MUMBA SUPPORTS EUTHINI RURAL HEALTH CENTRE WITH K4.4 MILLION ESCOM PAYMENT

Malawi Cables October 5, 2026
1000115715
  • Latest

APOLISI KU LILONGWE AMANGA BAMBO WAZAKA 53 PA MLANDU WOTHYOLA NDI KUFUNA KUBA ZITSULO KU KAMPANI YA CHASER CONSTRUCTION KU AREA 28

Andy Ten October 5, 2026
1000115652
  • Latest

TILEMBA NTCHITO APHUNZITSI 1,100 TELEMU INO- BRIGHT MSAKA

Andy Ten October 5, 2026
IMG_7312
  • Latest

ADMARC CASHGATE: CEO BOTOLO SPENDS K40MILLION FOR ACCOMMODATION

Malawi Cables October 5, 2026
Copyright © 2026 All rights reserved. | ReviewNews by AF themes.
%d