Skip to content

Malawi Cables Online

We Report the Future — the Only Trusted Source of News with a Difference

Primary Menu
  • Home
  • Latest
  • News
  • Breaking News
  • Religion
  • Economics
  • Politics
  • Sports
  • Home
  • Blog
  • Home
  • Latest
  • APOLISI KU CHIRADZULU AMANGA ISAAC PHAKALA CHIFUKWA CHOLOWELERA MKANGANO WA M’BANJA MPAKA KUPHA MWINI MKAZI
  • Latest

APOLISI KU CHIRADZULU AMANGA ISAAC PHAKALA CHIFUKWA CHOLOWELERA MKANGANO WA M’BANJA MPAKA KUPHA MWINI MKAZI

Andy Ten August 25, 2026 (Last updated: August 25, 2026)

Bambo Isaac Phakala awamanga ku Chiradzulu powaganizila kuti analowelera mkangano wa m’banja mpaka kupha mwamuna yemwe anali mwini mkazi.

Malingana ndi Ofalitsa Nkhani za a Polisi m’bomali a Hubert Mwangoka, malemuwa amamenyana ndi mkazi wawo yemwe ndiwoyembekezera ndipo anamuvulaza kwambiri ndipo anamutengela kuchipatala.

Mwangoka wati atabwerako kuchipatalako woganiziridwayo anapita kunyumba komwe amakadzuzula malemuwo kuti asamamenye akazi awo. Izi akuti sizinasangalase malemuwo ndipo ndewu inayambika

Apa woganizilidwayu anatenga mpeni ndibaya nawo mwini mkaziyo pafupi ndi khutu.

Atathamanga nawo kuchipatala malemuwo anamwalira akulandira thandizo lachipatala.

A Phakala akuyembekezereka kukaonekela ku bwalo la milandu posachedwa kumene akayankhe mulando umene apalamulawu.

About the Author

Andy Ten

Editor

Journalist from Mangochi former student and University of Malawi, The Polytechnic

View All Posts

Like this:

Like Loading…

Related

Post navigation

Previous: 14 Foreigners Deported For Violating Malawi’s Immigration Laws
Next: 35 YEARS OLD MAN DIED OF ELECTROCUTION IN MANGOCHI IN ATTEMPT TO REMOVE ELECTRICAL WIRE

Related Stories

1000121290
  • Latest

MV Chambo Sitima ya Pa Madzi Ya Ku Mozambique Yapsa Itayaka Moto Pa Nyanja ya Malawi Mbali ya Tanzania

Andy Ten October 11, 2026
1000121313
  • Latest

TWO MEN ARRESTED IN MZUZU IN CONNECTION WITH A MURDER OF FOUR YEARS OLD GIRL

Andy Ten October 11, 2026
1000120578
  • Latest

APOLISI KU NTCHISI AMANGA MAYI WINA KAAMBA KOPHA MWANA WAKE WONGOBADWA KUMENE

Andy Ten October 10, 2026

Recent Posts

  • MV Chambo Sitima ya Pa Madzi Ya Ku Mozambique Yapsa Itayaka Moto Pa Nyanja ya Malawi Mbali ya Tanzania
  • TWO MEN ARRESTED IN MZUZU IN CONNECTION WITH A MURDER OF FOUR YEARS OLD GIRL
  • APOLISI KU NTCHISI AMANGA MAYI WINA KAAMBA KOPHA MWANA WAKE WONGOBADWA KUMENE
  • SCORCHERS YADYA MWA ZIMBABWE 2 KWA DUU
  • AKASEWEDZE JELE ZAKA KHUMI KOMANSO ZISANU KAAMBA KOZEMBETSA MWANA KUTI AMUGULITSE

Recent Comments

No comments to show.

Archives

  • October 2026
  • September 2026
  • August 2026
  • July 2026
  • June 2026
  • May 2026
  • April 2026
  • March 2026
  • February 2026
  • January 2026
  • December 2025

Categories

  • Breaking News
  • Economics
  • Home
  • Latest
  • News
  • Politics
  • Religion
  • Sports

You May Have Missed

1000121290
  • Latest

MV Chambo Sitima ya Pa Madzi Ya Ku Mozambique Yapsa Itayaka Moto Pa Nyanja ya Malawi Mbali ya Tanzania

Andy Ten October 11, 2026
1000121313
  • Latest

TWO MEN ARRESTED IN MZUZU IN CONNECTION WITH A MURDER OF FOUR YEARS OLD GIRL

Andy Ten October 11, 2026
1000120578
  • Latest

APOLISI KU NTCHISI AMANGA MAYI WINA KAAMBA KOPHA MWANA WAKE WONGOBADWA KUMENE

Andy Ten October 10, 2026
1000120069
  • Latest

SCORCHERS YADYA MWA ZIMBABWE 2 KWA DUU

Andy Ten October 9, 2026
Copyright © 2026 All rights reserved. | ReviewNews by AF themes.
%d