Skip to content

Malawi Cables Online

We Report the Future — the Only Trusted Source of News with a Difference

Primary Menu
  • Home
  • Latest
  • News
  • Breaking News
  • Religion
  • Economics
  • Politics
  • Sports
  • Home
  • Blog
  • Home
  • Latest
  • CAF YASANKHA WOYIMBIRA NDI OMUTHANDIZIRA AKE AKU GHANA KUTI NDIWO AZAYIMBIRE MASEWERO A MIGHTY WANDERERS NDI SIMBA MU CAF CHAMPIONS LEAGUE
  • Latest

CAF YASANKHA WOYIMBIRA NDI OMUTHANDIZIRA AKE AKU GHANA KUTI NDIWO AZAYIMBIRE MASEWERO A MIGHTY WANDERERS NDI SIMBA MU CAF CHAMPIONS LEAGUE

Andy Ten August 25, 2026 (Last updated: August 25, 2026)

Confederation of African Football (CAF) yasankha woyimbira wa FIFA wa m’dziko la Ghana a Charles Bulu, kuti ndiye adzaimbire masewero oyamba a CAF Champions league pakati pa matimu Mighty Wanderers ndi Simba Sporting Club yaku Tanzania pa 6 September 2026 pa bwalo la Bingu mu mzinda wa Lilongwe.

CAF lasankhanso Seth Abletor komanso Richard Kweku Nartey ochokera ku Ghana komweko kuti ndi amene adzathandizire woyimbirayu.

Bungweli laika a Grema Mohammed aku Nigeria kuti adzagwire ntchito ngati oyimbira wapadera pamasewerowa

Matimu a Wanderers ndi Simba Sporting Club adzakumananso pamasewero achibwereza pa 12 September 2026 m’dziko la Tanzania.

About the Author

Andy Ten

Editor

Journalist from Mangochi former student and University of Malawi, The Polytechnic

View All Posts

Like this:

Like Loading…

Related

Post navigation

Previous: SMEDI CEO Kachamba Bypasses IPDC in Vehicle Purchases , Hires Procurement Officer Fired for Fraud Elsewhere
Next: 14 Foreigners Deported For Violating Malawi’s Immigration Laws

Related Stories

1000120069
  • Latest

SCORCHERS YADYA MWA ZIMBABWE 2 KWA DUU

Andy Ten October 9, 2026
1000118930
  • Latest

AKASEWEDZE JELE ZAKA KHUMI KOMANSO ZISANU KAAMBA KOZEMBETSA MWANA KUTI AMUGULITSE

Andy Ten October 8, 2026
1000118781
  • Latest

M’BUSA MEDRAN CHIRWA AMUMANGA KU DOWA KUTSATILA IMFA YA TATHOKOZA SALIMU YEMWE ANKAGWIRA NTCHITO KU FDH BANK

Andy Ten October 8, 2026

Recent Posts

  • SCORCHERS YADYA MWA ZIMBABWE 2 KWA DUU
  • AKASEWEDZE JELE ZAKA KHUMI KOMANSO ZISANU KAAMBA KOZEMBETSA MWANA KUTI AMUGULITSE
  • M’BUSA MEDRAN CHIRWA AMUMANGA KU DOWA KUTSATILA IMFA YA TATHOKOZA SALIMU YEMWE ANKAGWIRA NTCHITO KU FDH BANK
  • China Civils Gets MK 260 Bn New Project Despite Unfinished Kaunda , Lirangwe-Chingeni-Machinga Roads.
  • Roads Authority Issued Notice Of Intention To Award K587 Billion Contracts To Two Companies For Chiweta-Karonga Road Rehabilitation Project

Recent Comments

No comments to show.

Archives

  • October 2026
  • September 2026
  • August 2026
  • July 2026
  • June 2026
  • May 2026
  • April 2026
  • March 2026
  • February 2026
  • January 2026
  • December 2025

Categories

  • Breaking News
  • Economics
  • Home
  • Latest
  • News
  • Politics
  • Religion
  • Sports

You May Have Missed

1000120069
  • Latest

SCORCHERS YADYA MWA ZIMBABWE 2 KWA DUU

Andy Ten October 9, 2026
1000118930
  • Latest

AKASEWEDZE JELE ZAKA KHUMI KOMANSO ZISANU KAAMBA KOZEMBETSA MWANA KUTI AMUGULITSE

Andy Ten October 8, 2026
1000118781
  • Latest

M’BUSA MEDRAN CHIRWA AMUMANGA KU DOWA KUTSATILA IMFA YA TATHOKOZA SALIMU YEMWE ANKAGWIRA NTCHITO KU FDH BANK

Andy Ten October 8, 2026
ccec 2022
  • Economics
  • Latest

China Civils Gets MK 260 Bn New Project Despite Unfinished Kaunda , Lirangwe-Chingeni-Machinga Roads.

Malawi Cables October 7, 2026
Copyright © 2026 All rights reserved. | ReviewNews by AF themes.
%d