Skip to content

Malawi Cables Online

We Report the Future — the Only Trusted Source of News with a Difference

Primary Menu
  • Home
  • Latest
  • News
  • Breaking News
  • Religion
  • Economics
  • Politics
  • Sports
  • Home
  • Latest
  • AMAYI ATATU AMANGIDWA KU LILONGWE KAAMBA KOBISA KUBADWA KWAMWANA KOMANSO KUMUPONYA MWANAYO MUMTSINJE
  • Latest

AMAYI ATATU AMANGIDWA KU LILONGWE KAAMBA KOBISA KUBADWA KWAMWANA KOMANSO KUMUPONYA MWANAYO MUMTSINJE

Andy Ten November 2, 2026 (Last updated: November 2, 2026)

Apolisi m’boma la Lilongwe amanga amayi atatu powaganizira kuti anabisa kubadwa kwa mwana komanso kumuponya mumtsinje wa Lilongwe, m’dera la Mgubo, ku Chiwamba.

Mneneri wa apolisi a ku Kanengo, Sub Inspector Macfarlen Mseteka, amayi atatuwo ndi a Ivy Lyson azaka 26, a Mulitani Chotsani azaka 31, komanso a Mary Santhe azaka 40, onse ochokera m’mudzi wa Mgubo, kwa Mfumu Yaikulu Chimutu.

Apolisi ati pa 1 November 2026, anthu a m’deralo anapeza mwana wa tsiku limodzi akuyandama mumtsinje wa Lilongwe.

Iwo anati ana omwe ankasambira mumtsinjewo ndi omwe anapeza mwanayo ndipo anauza anthu ena, omwe anakafotokozera apolisi a ku Kanengo.

Mtseteka wati kafukufuku wa apolisi wasonyeza kuti Lyson anali ndi pakati pa miyezi yoposera isanu ndipo pa 31 October 2026 anayamba kuona zizindikiro zofuna kubereka.

Lyson anaitanitsa mnansi wake, Chotsani, komanso agogo ake aakazi, Santhe, kuti amuthandize pobereka.

Apolisi ati mwanayo atabadwa, amayiwa anapeza kuti wamwalira ndipo anagwirizana kubisa nkhaniyi chifukwa panalibe mwamuna amene akanatenga udindo pa mwanayo zomwe zinapangitsa kuti amponye mumtsinje wa Lilongwe.

Lyson anauza apolisi kuti amayi awiri achikulirewo ndi omwe anamulangiza kuti amuponye mwanayo mumtsinjewo ponena kuti mwamuna yemwe ankamuganizira kuti ndi yemwe anamupatsa mimba anali ataikana kale.

About the Author

Andy Ten

Editor

Journalist from Mangochi former student and University of Malawi, The Polytechnic

View All Posts

Like this:

Like Loading…

Related

Post navigation

Previous: MOTORIST LORDMARLVEN NECHAVAVA DEMAND K297.8 MILLION AND WRITTEN APOLOGY FROM BLANTYRE CITY MAYOR JOMO OSMAN
Next: A GIFT CHISUSU MHONE TSOPANO NDI AMENE AZILANKHULIRA BUNGWE LA ACB

Related Stories

1793612777667
  • Latest

A GIFT CHISUSU MHONE TSOPANO NDI AMENE AZILANKHULIRA BUNGWE LA ACB

Andy Ten November 2, 2026
1793606171974
  • Latest

MOTORIST LORDMARLVEN NECHAVAVA DEMAND K297.8 MILLION AND WRITTEN APOLOGY FROM BLANTYRE CITY MAYOR JOMO OSMAN

Andy Ten November 2, 2026
IMG_8204
  • Latest

EXPLOITATION AT KAYELEKERA URANIUM MINE: MALAWIAN WORKERS CRY OUT OVER ABUSE, LOW WAGES AND LABOUR RIGHTS VIOLATIONS

Malawi Cables November 2, 2026

Recent Posts

  • A GIFT CHISUSU MHONE TSOPANO NDI AMENE AZILANKHULIRA BUNGWE LA ACB
  • AMAYI ATATU AMANGIDWA KU LILONGWE KAAMBA KOBISA KUBADWA KWAMWANA KOMANSO KUMUPONYA MWANAYO MUMTSINJE
  • MOTORIST LORDMARLVEN NECHAVAVA DEMAND K297.8 MILLION AND WRITTEN APOLOGY FROM BLANTYRE CITY MAYOR JOMO OSMAN
  • EXPLOITATION AT KAYELEKERA URANIUM MINE: MALAWIAN WORKERS CRY OUT OVER ABUSE, LOW WAGES AND LABOUR RIGHTS VIOLATIONS
  • PRESIDENT MUTHARIKA RETURNS HOME FOLLOWING PRIVATE VISIT TO SOUTH AFRICA

Recent Comments

No comments to show.

Archives

  • November 2026
  • October 2026
  • September 2026
  • August 2026
  • July 2026
  • June 2026
  • May 2026
  • April 2026
  • March 2026
  • February 2026
  • January 2026
  • December 2025

Categories

  • Breaking News
  • Economics
  • Home
  • Latest
  • News
  • Politics
  • Religion
  • Sports

You May Have Missed

1793612777667
  • Latest

A GIFT CHISUSU MHONE TSOPANO NDI AMENE AZILANKHULIRA BUNGWE LA ACB

Andy Ten November 2, 2026
Screenshot_20261102_112012_Lite
  • Latest

AMAYI ATATU AMANGIDWA KU LILONGWE KAAMBA KOBISA KUBADWA KWAMWANA KOMANSO KUMUPONYA MWANAYO MUMTSINJE

Andy Ten November 2, 2026
1793606171974
  • Latest

MOTORIST LORDMARLVEN NECHAVAVA DEMAND K297.8 MILLION AND WRITTEN APOLOGY FROM BLANTYRE CITY MAYOR JOMO OSMAN

Andy Ten November 2, 2026
IMG_8204
  • Latest

EXPLOITATION AT KAYELEKERA URANIUM MINE: MALAWIAN WORKERS CRY OUT OVER ABUSE, LOW WAGES AND LABOUR RIGHTS VIOLATIONS

Malawi Cables November 2, 2026
Copyright © 2026 All rights reserved. | Malawi Cables Online by Cables Technologies.
%d