Skip to content

Malawi Cables Online

We Report the Future — the Only Trusted Source of News with a Difference

Primary Menu
  • Home
  • Latest
  • News
  • Breaking News
  • Religion
  • Economics
  • Politics
  • Sports
  • Home
  • Latest
  • A GIFT CHISUSU MHONE TSOPANO NDI AMENE AZILANKHULIRA BUNGWE LA ACB
  • Latest

A GIFT CHISUSU MHONE TSOPANO NDI AMENE AZILANKHULIRA BUNGWE LA ACB

Andy Ten November 2, 2026 (Last updated: November 2, 2026)

Bungwe lothana ndi katangale ndi ziphuphu la Anti-Corruption Bureau (ACB) lalengeza kuti Gift Chisusu Mhone ndi yemwe tsopano azilankhulira bungwe kuyambila pa 1 November 2026.

Izi azilengedza kudzera mu kalata yomwe wasayinila ndi wogwirizira udindo wa mkulu wa ACB Gabriel Chembezi yomwe yati Mhone yemwe ndi mkulu woona za maphunziro ku bungweli tsopano adzigwira ntchito zonse za ku nthambi yofalitsa ma uthenga ku ACB.

Chembezi wati Mhone walowa mmalo mwa Jacqueline Ngongonda yemwe wakhala akulankhulira bungweli kwa zaka zinayi.

Kalatayi yati a Ngongonda agwira ntchito ku bungweli kwa zaka zinayi ngati mneneri wake ndipo yawayamikila pa ntchito yotamandika yomwe akhala akugwira ku bungweli.

About the Author

Andy Ten

Editor

Journalist from Mangochi former student and University of Malawi, The Polytechnic

View All Posts

Like this:

Like Loading…

Related

Post navigation

Previous: AMAYI ATATU AMANGIDWA KU LILONGWE KAAMBA KOBISA KUBADWA KWAMWANA KOMANSO KUMUPONYA MWANAYO MUMTSINJE

Related Stories

Screenshot_20261102_112012_Lite
  • Latest

AMAYI ATATU AMANGIDWA KU LILONGWE KAAMBA KOBISA KUBADWA KWAMWANA KOMANSO KUMUPONYA MWANAYO MUMTSINJE

Andy Ten November 2, 2026
1793606171974
  • Latest

MOTORIST LORDMARLVEN NECHAVAVA DEMAND K297.8 MILLION AND WRITTEN APOLOGY FROM BLANTYRE CITY MAYOR JOMO OSMAN

Andy Ten November 2, 2026
IMG_8204
  • Latest

EXPLOITATION AT KAYELEKERA URANIUM MINE: MALAWIAN WORKERS CRY OUT OVER ABUSE, LOW WAGES AND LABOUR RIGHTS VIOLATIONS

Malawi Cables November 2, 2026

Recent Posts

  • A GIFT CHISUSU MHONE TSOPANO NDI AMENE AZILANKHULIRA BUNGWE LA ACB
  • AMAYI ATATU AMANGIDWA KU LILONGWE KAAMBA KOBISA KUBADWA KWAMWANA KOMANSO KUMUPONYA MWANAYO MUMTSINJE
  • MOTORIST LORDMARLVEN NECHAVAVA DEMAND K297.8 MILLION AND WRITTEN APOLOGY FROM BLANTYRE CITY MAYOR JOMO OSMAN
  • EXPLOITATION AT KAYELEKERA URANIUM MINE: MALAWIAN WORKERS CRY OUT OVER ABUSE, LOW WAGES AND LABOUR RIGHTS VIOLATIONS
  • PRESIDENT MUTHARIKA RETURNS HOME FOLLOWING PRIVATE VISIT TO SOUTH AFRICA

Recent Comments

No comments to show.

Archives

  • November 2026
  • October 2026
  • September 2026
  • August 2026
  • July 2026
  • June 2026
  • May 2026
  • April 2026
  • March 2026
  • February 2026
  • January 2026
  • December 2025

Categories

  • Breaking News
  • Economics
  • Home
  • Latest
  • News
  • Politics
  • Religion
  • Sports

You May Have Missed

1793612777667
  • Latest

A GIFT CHISUSU MHONE TSOPANO NDI AMENE AZILANKHULIRA BUNGWE LA ACB

Andy Ten November 2, 2026
Screenshot_20261102_112012_Lite
  • Latest

AMAYI ATATU AMANGIDWA KU LILONGWE KAAMBA KOBISA KUBADWA KWAMWANA KOMANSO KUMUPONYA MWANAYO MUMTSINJE

Andy Ten November 2, 2026
1793606171974
  • Latest

MOTORIST LORDMARLVEN NECHAVAVA DEMAND K297.8 MILLION AND WRITTEN APOLOGY FROM BLANTYRE CITY MAYOR JOMO OSMAN

Andy Ten November 2, 2026
IMG_8204
  • Latest

EXPLOITATION AT KAYELEKERA URANIUM MINE: MALAWIAN WORKERS CRY OUT OVER ABUSE, LOW WAGES AND LABOUR RIGHTS VIOLATIONS

Malawi Cables November 2, 2026
Copyright © 2026 All rights reserved. | Malawi Cables Online by Cables Technologies.
%d