Likoma Island Sold By Chakwera, MCP To German Gambler

After failing on 20 billion project to print Chelsea Jerseys, Malawi Congress Party led by Chakwera is at it again, they have initiated sale of Likoma island to a German gambling kingpin.

  1. Likoma Island ikhala mmanja mwa ayuda kwa zaka 99
  2. Anthu osachepera 10,000 athamangitsidwa ku Likoma Island, apeze kokhala kwina
  3. Muyudayu akuti samalipira msonkho ulionse.
  4. Ndipo pa island pasabwere competitor, akhalepo yekha yekha island yonse
  5. Malamulo amalawi samagwira ntchito ku island, ikhala dziko palokha ndi malamulo ake
  6. A tourism apangitsa lease island ya Likoma koma a lands sakudziwa kalikonse, sanapangidwenso consult, kupangitsa lease island without involving ministry of lands ndi mafumu
  7. Mtengo ogulitsira island sukudziwika, akudziwa ndi nduna ya tourism
  8. Likoma Island will be no go zone for land owners, kaya kuli manda awo kaya kuli chani, asadzabwere
  9. Mwini wa island adzabweretsa security yake, apolisi amalawi sadzakhala ndi mphanvu yogwira ntchito Ku island kwa zaka 99
  10. Mwini island adzakhala president, adzapanga malamulo ake, adzayendetsa island momwe akufunira popanda mfwi mfwi mfwi

Inu satana kwake nkupha, kuba ndi kuononga

Malawi Cables

Malawi Cables is a dedicated news platform providing timely and accurate coverage of events and stories from Malawi and beyond. The website aims to inform and engage readers by delivering powerful analysis and reporting.

Related Posts

Leave a Reply

You Missed

SLEEPY, PUPPET CHAKWERA BOWS TO SON’S PRESSURE, EYES MUMBA AS RUNNING MATE, 2030 SUCCESSOR

SLEEPY, PUPPET CHAKWERA BOWS TO SON’S PRESSURE, EYES MUMBA AS RUNNING MATE, 2030 SUCCESSOR

Usi Sparks Outrage at Mulli Funeral: Accused of Turning Burial into Political Stage

Usi Sparks Outrage at Mulli Funeral: Accused of Turning Burial into Political Stage

Mutharika Criticizes Faith Community’s Silence on Governance Amid National Hardships

Mutharika Criticizes Faith Community’s Silence on Governance Amid National Hardships

“Chakwera Can’t Fire Me,” Boasts Chimwendo Banda

“Chakwera Can’t Fire Me,” Boasts Chimwendo Banda