Lero bungwe la Dr Jane Ansah Foundation lafika ku Kasungu kudzapereka chithandizo kwa anthu ovutika komanso osowa. Anthuwa alandira thandizo losiyanasiyana lomwe lathandiza kubweretsa chisomo, chimwemwe ndi chiyembekezo m’miyoyo yawo.
M’zithuzi: momwe anthu analandirila thandizoli ndi chisangalalo chachikulu pamodzi ndi ntchito zabwino zomwe bungweli lachita m’dera la Kasungu.