Skip to content

Malawi Cables Online

We Report the Future — the Only Trusted Source of News with a Difference

Primary Menu
  • Home
  • Latest
  • News
  • Breaking News
  • Religion
  • Economics
  • Politics
  • Sports
  • Home
  • Blog
  • Home
  • Latest
  • SCORCHERS YADYA MWA ZIMBABWE 2 KWA DUU
  • Latest

SCORCHERS YADYA MWA ZIMBABWE 2 KWA DUU

Andy Ten October 9, 2026 (Last updated: October 9, 2026)

Timu yampira wamiyendo ya dziko lino ya osewera akazi ya Scorchers yagonjetsa timu ya Zimbabwe ndizigoli ziwili kwachilowere pa bwalo la Bingu mu mzinda wa Lilongwe

Temwa Chawinga anagoletsa chigoli choyamba pa mphindi 33 zachigawo choyamba mothandizidwa ndi Tabitha Chawinga ndipo chigawochi chinathera 1 -0.

M’chigawo chachiwiri Tabitha Chawinga anawonetsetsa kuti chikondwerero cha a Malawi chikhazikike pamene anamwetsa chigoli chachiwiri pa mphindi 50 kuti Malawi itsogole ndizigoli ziwiri.

Scorchers inasewela bwino mzigawo zonse ziwiri kufikila woyimbila masewerowa anaimba khelele lomalidza kuti Zimbabwe yafera koyenda.

About the Author

Andy Ten

Editor

Journalist from Mangochi former student and University of Malawi, The Polytechnic

View All Posts

Like this:

Like Loading…

Related

Post navigation

Previous: AKASEWEDZE JELE ZAKA KHUMI KOMANSO ZISANU KAAMBA KOZEMBETSA MWANA KUTI AMUGULITSE

Related Stories

1000118930
  • Latest

AKASEWEDZE JELE ZAKA KHUMI KOMANSO ZISANU KAAMBA KOZEMBETSA MWANA KUTI AMUGULITSE

Andy Ten October 8, 2026
1000118781
  • Latest

M’BUSA MEDRAN CHIRWA AMUMANGA KU DOWA KUTSATILA IMFA YA TATHOKOZA SALIMU YEMWE ANKAGWIRA NTCHITO KU FDH BANK

Andy Ten October 8, 2026
ccec 2022
  • Economics
  • Latest

China Civils Gets MK 260 Bn New Project Despite Unfinished Kaunda , Lirangwe-Chingeni-Machinga Roads.

Malawi Cables October 7, 2026

Recent Posts

  • SCORCHERS YADYA MWA ZIMBABWE 2 KWA DUU
  • AKASEWEDZE JELE ZAKA KHUMI KOMANSO ZISANU KAAMBA KOZEMBETSA MWANA KUTI AMUGULITSE
  • M’BUSA MEDRAN CHIRWA AMUMANGA KU DOWA KUTSATILA IMFA YA TATHOKOZA SALIMU YEMWE ANKAGWIRA NTCHITO KU FDH BANK
  • China Civils Gets MK 260 Bn New Project Despite Unfinished Kaunda , Lirangwe-Chingeni-Machinga Roads.
  • Roads Authority Issued Notice Of Intention To Award K587 Billion Contracts To Two Companies For Chiweta-Karonga Road Rehabilitation Project

Recent Comments

No comments to show.

Archives

  • October 2026
  • September 2026
  • August 2026
  • July 2026
  • June 2026
  • May 2026
  • April 2026
  • March 2026
  • February 2026
  • January 2026
  • December 2025

Categories

  • Breaking News
  • Economics
  • Home
  • Latest
  • News
  • Politics
  • Religion
  • Sports

You May Have Missed

1000120069
  • Latest

SCORCHERS YADYA MWA ZIMBABWE 2 KWA DUU

Andy Ten October 9, 2026
1000118930
  • Latest

AKASEWEDZE JELE ZAKA KHUMI KOMANSO ZISANU KAAMBA KOZEMBETSA MWANA KUTI AMUGULITSE

Andy Ten October 8, 2026
1000118781
  • Latest

M’BUSA MEDRAN CHIRWA AMUMANGA KU DOWA KUTSATILA IMFA YA TATHOKOZA SALIMU YEMWE ANKAGWIRA NTCHITO KU FDH BANK

Andy Ten October 8, 2026
ccec 2022
  • Economics
  • Latest

China Civils Gets MK 260 Bn New Project Despite Unfinished Kaunda , Lirangwe-Chingeni-Machinga Roads.

Malawi Cables October 7, 2026
Copyright © 2026 All rights reserved. | ReviewNews by AF themes.
%d