Skip to content

Malawi Cables Online

We Report the Future — the Only Trusted Source of News with a Difference

Primary Menu
  • Home
  • Latest
  • News
  • Breaking News
  • Religion
  • Economics
  • Politics
  • Sports
  • Home
  • Blog
  • Home
  • Latest
  • APOLISI KU NTCHISI AMANGA MAYI WINA KAAMBA KOPHA MWANA WAKE WONGOBADWA KUMENE
  • Latest

APOLISI KU NTCHISI AMANGA MAYI WINA KAAMBA KOPHA MWANA WAKE WONGOBADWA KUMENE

Andy Ten October 10, 2026 (Last updated: October 10, 2026)

Apolisi m’boma la Ntchisi amanga mayi wina a Labeka Wilson a zaka 35 powaganizira kuti apha mwana wawo ongobadwa kumene pomukwilira mu dothi.

Malingana ndi malipoti mayi Labeka Wilson anakwilira mwanayu ku tchire komwe anachila alikotola nkhuni.

A Wilson anachilira ku tchireku matenda atawayamba ndipo anauza a nzawo kuti atsogole kaamba koti amafuna azitolabe nkhuni.

Apa mpomwe anachira ku tchire konko, kenako anapha mwanayo nkumukwilira.

Anthu a mmudzi ndi omwe anawadabwa kuti mimba yachoka, ndipo atapanikiza ndi mafunso mpomwe anavomela kuti achira koma mwanayo amukwilira.

About the Author

Andy Ten

Editor

Journalist from Mangochi former student and University of Malawi, The Polytechnic

View All Posts

Like this:

Like Loading…

Related

Post navigation

Previous: SCORCHERS YADYA MWA ZIMBABWE 2 KWA DUU

Related Stories

1000120069
  • Latest

SCORCHERS YADYA MWA ZIMBABWE 2 KWA DUU

Andy Ten October 9, 2026
1000118930
  • Latest

AKASEWEDZE JELE ZAKA KHUMI KOMANSO ZISANU KAAMBA KOZEMBETSA MWANA KUTI AMUGULITSE

Andy Ten October 8, 2026
1000118781
  • Latest

M’BUSA MEDRAN CHIRWA AMUMANGA KU DOWA KUTSATILA IMFA YA TATHOKOZA SALIMU YEMWE ANKAGWIRA NTCHITO KU FDH BANK

Andy Ten October 8, 2026

Recent Posts

  • APOLISI KU NTCHISI AMANGA MAYI WINA KAAMBA KOPHA MWANA WAKE WONGOBADWA KUMENE
  • SCORCHERS YADYA MWA ZIMBABWE 2 KWA DUU
  • AKASEWEDZE JELE ZAKA KHUMI KOMANSO ZISANU KAAMBA KOZEMBETSA MWANA KUTI AMUGULITSE
  • M’BUSA MEDRAN CHIRWA AMUMANGA KU DOWA KUTSATILA IMFA YA TATHOKOZA SALIMU YEMWE ANKAGWIRA NTCHITO KU FDH BANK
  • China Civils Gets MK 260 Bn New Project Despite Unfinished Kaunda , Lirangwe-Chingeni-Machinga Roads.

Recent Comments

No comments to show.

Archives

  • October 2026
  • September 2026
  • August 2026
  • July 2026
  • June 2026
  • May 2026
  • April 2026
  • March 2026
  • February 2026
  • January 2026
  • December 2025

Categories

  • Breaking News
  • Economics
  • Home
  • Latest
  • News
  • Politics
  • Religion
  • Sports

You May Have Missed

1000120578
  • Latest

APOLISI KU NTCHISI AMANGA MAYI WINA KAAMBA KOPHA MWANA WAKE WONGOBADWA KUMENE

Andy Ten October 10, 2026
1000120069
  • Latest

SCORCHERS YADYA MWA ZIMBABWE 2 KWA DUU

Andy Ten October 9, 2026
1000118930
  • Latest

AKASEWEDZE JELE ZAKA KHUMI KOMANSO ZISANU KAAMBA KOZEMBETSA MWANA KUTI AMUGULITSE

Andy Ten October 8, 2026
1000118781
  • Latest

M’BUSA MEDRAN CHIRWA AMUMANGA KU DOWA KUTSATILA IMFA YA TATHOKOZA SALIMU YEMWE ANKAGWIRA NTCHITO KU FDH BANK

Andy Ten October 8, 2026
Copyright © 2026 All rights reserved. | ReviewNews by AF themes.
%d