Skip to content

Malawi Cables Online

We Report the Future — the Only Trusted Source of News with a Difference

Primary Menu
  • Home
  • Latest
  • News
  • Breaking News
  • Religion
  • Economics
  • Politics
  • Sports
  • Home
  • Latest
  • BAMBO WAZAKA 39 WAFA ATAZIMANGILIRA ALI M’CHITOKOSI CHA POLISI KU KASUNGU
  • Latest

BAMBO WAZAKA 39 WAFA ATAZIMANGILIRA ALI M’CHITOKOSI CHA POLISI KU KASUNGU

Andy Ten November 16, 2026 (Last updated: November 16, 2026)

Apolisi m’boma la Kasungu atsimikiza za imfa ya a Mustafa Nthandi azaka 39, omwe amaganizilidwa kuti anaba katundu pa malo a ntchito, ndipo afa pozimangilira ali m’chitokosi cha apolisi.

Malinga ndi woyankhulira apolisi m’chigawo chapakati chakummawa, Esther Mkwanda, izi zachitika lero ku mmawaku pomwe a Nthandi anapemba kuti akazithandize.

Mkwanda wati Nthandi yemwe amachokera mdera la Chilanga, mfumu yaikulu Kaomba m’boma lomweli anagwiritsa ntchito malaya omwe anavala pozimangilira.

About the Author

Andy Ten

Editor

Journalist from Mangochi former student and University of Malawi, The Polytechnic

View All Posts

Like this:

Like Loading…

Related

Post navigation

Previous: BOMA ALIPEMPHA KUTI LICHITEPO KANTHU PA VUTO LAKUZIMAZIMA KWA MAGESI MZIPATALA DZIKO MUNO
Next: CHIPUNGU REPRESENTS MALAWI AS SHE JOINS 20 REGIONAL STATES TO ADVANCE LAND GOVERNANCE AND GEOSPATIAL DEVELOPMENT

Related Stories

IMG_8643
  • Economics
  • Latest

CHIPUNGU REPRESENTS MALAWI AS SHE JOINS 20 REGIONAL STATES TO ADVANCE LAND GOVERNANCE AND GEOSPATIAL DEVELOPMENT

Malawi Cables November 17, 2026
1794825127490
  • Latest

BOMA ALIPEMPHA KUTI LICHITEPO KANTHU PA VUTO LAKUZIMAZIMA KWA MAGESI MZIPATALA DZIKO MUNO

Andy Ten November 16, 2026
1794592131442
  • Latest

POLICE OFFICER DIED ON DUTY IN BLANTYRE

Andy Ten November 13, 2026

Recent Posts

  • CHIPUNGU REPRESENTS MALAWI AS SHE JOINS 20 REGIONAL STATES TO ADVANCE LAND GOVERNANCE AND GEOSPATIAL DEVELOPMENT
  • BAMBO WAZAKA 39 WAFA ATAZIMANGILIRA ALI M’CHITOKOSI CHA POLISI KU KASUNGU
  • BOMA ALIPEMPHA KUTI LICHITEPO KANTHU PA VUTO LAKUZIMAZIMA KWA MAGESI MZIPATALA DZIKO MUNO
  • POLICE OFFICER DIED ON DUTY IN BLANTYRE
  • THE GREAT CONTROVERSY ! DPP PROMISED FOREX, SOLUTIONS IN SIX MONTHS. NOW WANTS TWO YEARS, PATIENCE

Categories

  • Breaking News
  • Economics
  • Home
  • Latest
  • News
  • Politics
  • Religion
  • Sports

You May Have Missed

IMG_8643
  • Economics
  • Latest

CHIPUNGU REPRESENTS MALAWI AS SHE JOINS 20 REGIONAL STATES TO ADVANCE LAND GOVERNANCE AND GEOSPATIAL DEVELOPMENT

Malawi Cables November 17, 2026
1794826202493
  • Latest

BAMBO WAZAKA 39 WAFA ATAZIMANGILIRA ALI M’CHITOKOSI CHA POLISI KU KASUNGU

Andy Ten November 16, 2026
1794825127490
  • Latest

BOMA ALIPEMPHA KUTI LICHITEPO KANTHU PA VUTO LAKUZIMAZIMA KWA MAGESI MZIPATALA DZIKO MUNO

Andy Ten November 16, 2026
1794592131442
  • Latest

POLICE OFFICER DIED ON DUTY IN BLANTYRE

Andy Ten November 13, 2026
Copyright © 2026 All rights reserved. | ReviewNews by AF themes.
%d