Skip to content

Malawi Cables Online

We Report the Future — the Only Trusted Source of News with a Difference

Primary Menu
  • Home
  • Latest
  • News
  • Breaking News
  • Religion
  • Economics
  • Politics
  • Sports
  • Home
  • Blog
  • Home
  • Latest
  • APOLISI KU BLANTYRE AMANGA AMUNA ASANU KAAMBA KOBA GALIMOTO KU PARISH YA LAWRENCE NKOKA
  • Latest

APOLISI KU BLANTYRE AMANGA AMUNA ASANU KAAMBA KOBA GALIMOTO KU PARISH YA LAWRENCE NKOKA

Andy Ten October 7, 2026 (Last updated: October 7, 2026)

Ku Blantyre apolisi amanga anthu asanu kamba kowaganizira kuti anathyola ndikuba galimoto ku Parish ya Lawrence Nkoka mwenzi wapitawu.

Malingana ndi m’neneri wa a polisi ku Blantyre a Mary Chiponda, anthuwa omwe ananyamula zikwanje anamangilira alonda awiri ndi kulowa m’nyumba ya bambo mfumu apa Parish ya Lawrence Nkoka a Samuel Zelengera.

A Chiponda ati anthuwa anaba galimoto ya mtundu wa Toyota Rav 4, kanema, Laptop ndi mafoni.

Malipoti amati galimoto lobedwalo linapezeka ku Soche kwa Manje m’mawa wapa 26 September 2026 koma mbava zimene zinaba galimotoli zinali zisanapezeke.

About the Author

Andy Ten

Editor

Journalist from Mangochi former student and University of Malawi, The Polytechnic

View All Posts

Like this:

Like Loading…

Related

Post navigation

Previous: MTSOGOLERI WA DZIKO LINO PRO PETER MUTHARIKA MUTHARIKA WACHOTSA A JOSEPH BONGOLOLO GONDWE PA UDINDO WAKE NGATI PARAMOUNT CHIEF CHIKULAMAYEMBE
Next: Roads Authority Issued Notice Of Intention To Award K587 Billion Contracts To Two Companies For Chiweta-Karonga Road Rehabilitation Project

Related Stories

ccec 2022
  • Economics
  • Latest

China Civils Gets MK 260 Bn New Project Despite Unfinished Kaunda , Lirangwe-Chingeni-Machinga Roads.

Malawi Cables October 7, 2026
1000118150-768x1024-1.jpg
  • Latest

Roads Authority Issued Notice Of Intention To Award K587 Billion Contracts To Two Companies For Chiweta-Karonga Road Rehabilitation Project

Andy Ten October 7, 2026
1000118065
  • Latest

MTSOGOLERI WA DZIKO LINO PRO PETER MUTHARIKA MUTHARIKA WACHOTSA A JOSEPH BONGOLOLO GONDWE PA UDINDO WAKE NGATI PARAMOUNT CHIEF CHIKULAMAYEMBE

Andy Ten October 7, 2026

Recent Posts

  • China Civils Gets MK 260 Bn New Project Despite Unfinished Kaunda , Lirangwe-Chingeni-Machinga Roads.
  • Roads Authority Issued Notice Of Intention To Award K587 Billion Contracts To Two Companies For Chiweta-Karonga Road Rehabilitation Project
  • APOLISI KU BLANTYRE AMANGA AMUNA ASANU KAAMBA KOBA GALIMOTO KU PARISH YA LAWRENCE NKOKA
  • MTSOGOLERI WA DZIKO LINO PRO PETER MUTHARIKA MUTHARIKA WACHOTSA A JOSEPH BONGOLOLO GONDWE PA UDINDO WAKE NGATI PARAMOUNT CHIEF CHIKULAMAYEMBE
  • AMUNJATA ATAGONA NDI MTSIKANA WACHICHEPELE KU BALAKA

Recent Comments

No comments to show.

Archives

  • October 2026
  • September 2026
  • August 2026
  • July 2026
  • June 2026
  • May 2026
  • April 2026
  • March 2026
  • February 2026
  • January 2026
  • December 2025

Categories

  • Breaking News
  • Economics
  • Home
  • Latest
  • News
  • Politics
  • Religion
  • Sports

You May Have Missed

ccec 2022
  • Economics
  • Latest

China Civils Gets MK 260 Bn New Project Despite Unfinished Kaunda , Lirangwe-Chingeni-Machinga Roads.

Malawi Cables October 7, 2026
1000118150-768x1024-1.jpg
  • Latest

Roads Authority Issued Notice Of Intention To Award K587 Billion Contracts To Two Companies For Chiweta-Karonga Road Rehabilitation Project

Andy Ten October 7, 2026
1000118115
  • Latest

APOLISI KU BLANTYRE AMANGA AMUNA ASANU KAAMBA KOBA GALIMOTO KU PARISH YA LAWRENCE NKOKA

Andy Ten October 7, 2026
1000118065
  • Latest

MTSOGOLERI WA DZIKO LINO PRO PETER MUTHARIKA MUTHARIKA WACHOTSA A JOSEPH BONGOLOLO GONDWE PA UDINDO WAKE NGATI PARAMOUNT CHIEF CHIKULAMAYEMBE

Andy Ten October 7, 2026
Copyright © 2026 All rights reserved. | ReviewNews by AF themes.
%d