Skip to content

Malawi Cables Online

We Report the Future — the Only Trusted Source of News with a Difference

Primary Menu
  • Home
  • Latest
  • News
  • Breaking News
  • Religion
  • Economics
  • Politics
  • Sports
  • Home
  • Blog
  • Home
  • Latest
  • AMUNJATA ATAGONA NDI MTSIKANA WACHICHEPELE KU BALAKA
  • Latest

AMUNJATA ATAGONA NDI MTSIKANA WACHICHEPELE KU BALAKA

Andy Ten October 7, 2026 (Last updated: October 7, 2026)

Apolisi ku Balaka amanga bambo wazaka 29 Sulaimana Rashid kamba kowaganizira kuti agona ndi mtsungwana wachichepele wazaka 14 atamunyengerera kuti amupatsa mankhwala azitsamba kuti azikakhoza bwino ku sukulu.

Malingana ndi Wofalisa nkhani za Polisi ku Balaka a Gladson M’bumpha oganizilidwawa anachita zosayenerazo ndi mwana wachichepeleyo nyumba mwawo lolemba sabata ino kwa Chendausiku m’bomali.

M’bumpha wati mayi wina ndiye anawona mtsungwanayu akutuluka nyumba mwa woganiziridwayu ndipo anakaziwitsa mayi ake amwanayu amene anamufutsa mwanayo ndipo anawulura kuti wachita zadama ndi bamboyo.

Apa nkhaniyi inakasiyidwa ku polisi ndipo apolisi adagwira ndikumanga woganiziridwayu.

Sulaimana Rashid amachokera Mudzi mwa Kaipakunja mdera ya Mfumu yaikulu Nsamala ku Balaka.

About the Author

Andy Ten

Editor

Journalist from Mangochi former student and University of Malawi, The Polytechnic

View All Posts

Like this:

Like Loading…

Related

Post navigation

Previous: Police Secretly Arrest, Release Shafiq Bemati Over Immigration Network: Duped Victims Of MK 150 Million
Next: MTSOGOLERI WA DZIKO LINO PRO PETER MUTHARIKA MUTHARIKA WACHOTSA A JOSEPH BONGOLOLO GONDWE PA UDINDO WAKE NGATI PARAMOUNT CHIEF CHIKULAMAYEMBE

Related Stories

ccec 2022
  • Economics
  • Latest

China Civils Gets MK 260 Bn New Project Despite Unfinished Kaunda , Lirangwe-Chingeni-Machinga Roads.

Malawi Cables October 7, 2026
1000118150-768x1024-1.jpg
  • Latest

Roads Authority Issued Notice Of Intention To Award K587 Billion Contracts To Two Companies For Chiweta-Karonga Road Rehabilitation Project

Andy Ten October 7, 2026
1000118115
  • Latest

APOLISI KU BLANTYRE AMANGA AMUNA ASANU KAAMBA KOBA GALIMOTO KU PARISH YA LAWRENCE NKOKA

Andy Ten October 7, 2026

Recent Posts

  • China Civils Gets MK 260 Bn New Project Despite Unfinished Kaunda , Lirangwe-Chingeni-Machinga Roads.
  • Roads Authority Issued Notice Of Intention To Award K587 Billion Contracts To Two Companies For Chiweta-Karonga Road Rehabilitation Project
  • APOLISI KU BLANTYRE AMANGA AMUNA ASANU KAAMBA KOBA GALIMOTO KU PARISH YA LAWRENCE NKOKA
  • MTSOGOLERI WA DZIKO LINO PRO PETER MUTHARIKA MUTHARIKA WACHOTSA A JOSEPH BONGOLOLO GONDWE PA UDINDO WAKE NGATI PARAMOUNT CHIEF CHIKULAMAYEMBE
  • AMUNJATA ATAGONA NDI MTSIKANA WACHICHEPELE KU BALAKA

Recent Comments

No comments to show.

Archives

  • October 2026
  • September 2026
  • August 2026
  • July 2026
  • June 2026
  • May 2026
  • April 2026
  • March 2026
  • February 2026
  • January 2026
  • December 2025

Categories

  • Breaking News
  • Economics
  • Home
  • Latest
  • News
  • Politics
  • Religion
  • Sports

You May Have Missed

ccec 2022
  • Economics
  • Latest

China Civils Gets MK 260 Bn New Project Despite Unfinished Kaunda , Lirangwe-Chingeni-Machinga Roads.

Malawi Cables October 7, 2026
1000118150-768x1024-1.jpg
  • Latest

Roads Authority Issued Notice Of Intention To Award K587 Billion Contracts To Two Companies For Chiweta-Karonga Road Rehabilitation Project

Andy Ten October 7, 2026
1000118115
  • Latest

APOLISI KU BLANTYRE AMANGA AMUNA ASANU KAAMBA KOBA GALIMOTO KU PARISH YA LAWRENCE NKOKA

Andy Ten October 7, 2026
1000118065
  • Latest

MTSOGOLERI WA DZIKO LINO PRO PETER MUTHARIKA MUTHARIKA WACHOTSA A JOSEPH BONGOLOLO GONDWE PA UDINDO WAKE NGATI PARAMOUNT CHIEF CHIKULAMAYEMBE

Andy Ten October 7, 2026
Copyright © 2026 All rights reserved. | ReviewNews by AF themes.
%d