Skip to content

Malawi Cables Online

We Report the Future — the Only Trusted Source of News with a Difference

Primary Menu
  • Home
  • Latest
  • News
  • Breaking News
  • Religion
  • Economics
  • Politics
  • Sports
  • Home
  • Blog
  • Home
  • Latest
  • Mukanadekha Bwana Chakwera Osati Kukhala Yaviyavi-Gerald Kampanikiza
  • Latest

Mukanadekha Bwana Chakwera Osati Kukhala Yaviyavi-Gerald Kampanikiza

Malawi Cables May 15, 2026 (Last updated: May 15, 2026)
Screenshot

Screenshot

Zachitika dzuro zija ndizinthu zosakhara bwino mpang’ono pomwe kutsira utsi watsabola okhetsa misozi kwa Mtsogoleri wakale wa dziko. Ine mkuwona kwanga ndikuti amene muli pafupi ndi Dr Lazarus McCarthy Chakwera munapanga mistake yayikulu kulora kuti iwo atuluke mkukakhara nawo pa dipiti umene uja.

Ku MCP mukuyenera kuyamba ndiyinu kuteteza a Chakwera kuposa wina aliyese mdziko muno, mukuyenera kudziwa kuti iwowo ndi Pangolin wanu ndipo mbali inayo imawawopabe.

Mkanakhara kuti ine ndafusidwa maganizo anga mkanati Bwana asapite kumeneko, bwanawa panopo aloreni azipita ma ulendo awo akunja, koma osati public gatherings ngati ya dzuro ija. President amene watuluka kumene amakhara akuwopedwa mpaka next general election.

Tiyeni tipite ku 2014, Dr Joyce Banda ataluza chisankho anavomeleza ndipo anapita kukakhara ku Nkhatabay. Atakharakhara anatuluka mdziko muno ndipo posafuna kuti Boma lotsogozedwa ndi Prof Arthur Peter Mutharika liziti akuwasokoneza iwo anakhakhara kaye kunja.

A Peter Mutharika ataluza 2020, zomwe iwo anavomeleza mkukakhara ku PAGE House ku Mangochi. Iwo amkadziwa kuti Boma lomwe lapambana mposavuta kuwapezera milandu, chomcho iwo sanakhare busy kuwonekera ku dziko ndipo adayamba kulankhura patadutsa nthawi ndipo ankalankhulira kunyumba kwawo kudzera muma kalata kapena kuyitanitsa msonkhano wa tolankhani.

A Mutharika amkadziwa kuti pano alibeso mphavu ngati president ndipo a police omwe aja amkawalemekeza pano sangawapatseso ulemu ngati omwe uja. Iwo adadziyikira nthawi yozayamba kutuluka uko akuwona anyamata awo onse a kumangidwa ndipo amkadziwa kuti tchire lomwe lidstsara anali iwowo.

Kumbukirani kuti there is a difference between Power and Authority, munthu ungathe kukhara ndi mphavu koma ulamuliro ulibe. Mukamayenda pa nsewu mumatha kupeza wa traffic ka mtsikana kochepa nyama kungokweza dzanja inu kuyimitsa galimoto chufukwa ali ndi Authority, ka mnyamata kakang’ono kumanga chi bouncer cha mphavu that’s Authority, Wina ungathe kukhara wa dzimphavu kukayima pa nsewu koma Authority ulibe akuwombapo ndithu. Boma lilllonse loti lalowa kumene komaso zambiri sizikuyenda bwino silingalore kuti pakakhare ulendo wa ndawala ngati umene umachitika dzuro uja, chifukwa kuthekera koyamba mademo kumakhara pafupi kwambiri.

I repeat protect Dr Lazarus McCarthy Chakwera at all times, he is your Pangolin, nthawi ikwana yokha yoti ayambe kutuluka panopo azingolankhura ali kunyumba basi.

About the Author

Malawi Cables

Administrator

Malawi Cables is a dedicated news platform committed to delivering timely, accurate, and credible coverage of events and stories from Malawi and beyond.We aim to inform, educate, and engage our readers through in-depth reporting, insightful analysis, and impactful storytelling that sets us apart.

Visit Website View All Posts

Like this:

Like Loading…

Related

Post navigation

Previous: “Munagula Teargas wambiri Kuposa chimanga”- Njawala Asambwadza MCP
Next: Malawi Bureau of Standards Goes Online

Related Stories

1000161687
  • Latest

EIGHT PEOPLE ARRESTED IN MANGOCHI IN CONNECTION TO VANDALISM OF CHILIPA POLICE UNIT AND COURT

Andy Ten September 3, 2026
IMG_6458
  • Latest

SPEAKER SAMEER SULEMAN DECLARES PARLIAMENT WILL STAND WITH MALAWIANS,BEGIN PROBES

Malawi Cables September 3, 2026
IMG_6457
  • Latest

VICE PRESIDENT ANSAH HOSTS AFRICAN BEAUTY QUEENS, CHAMPIONS REGIONAL CULTURAL COOPERATION

Malawi Cables September 3, 2026

Recent Posts

  • EIGHT PEOPLE ARRESTED IN MANGOCHI IN CONNECTION TO VANDALISM OF CHILIPA POLICE UNIT AND COURT
  • SPEAKER SAMEER SULEMAN DECLARES PARLIAMENT WILL STAND WITH MALAWIANS,BEGIN PROBES
  • VICE PRESIDENT ANSAH HOSTS AFRICAN BEAUTY QUEENS, CHAMPIONS REGIONAL CULTURAL COOPERATION
  • POLICE IN KARONGA ARRESTED A CHINESE NATIONAL FOR OPERATING ONLINE BUSINESS WITHOUT LICENCE
  • Mcdonald Mtetemera Appointed As Mighty Wanderers Acting Head Coach

Recent Comments

No comments to show.

Archives

  • September 2026
  • August 2026
  • July 2026
  • June 2026
  • May 2026
  • April 2026
  • March 2026
  • February 2026
  • January 2026
  • December 2025

Categories

  • Breaking News
  • Economics
  • Home
  • Latest
  • News
  • Politics
  • Religion
  • Sports

You May Have Missed

1000161687
  • Latest

EIGHT PEOPLE ARRESTED IN MANGOCHI IN CONNECTION TO VANDALISM OF CHILIPA POLICE UNIT AND COURT

Andy Ten September 3, 2026
IMG_6458
  • Latest

SPEAKER SAMEER SULEMAN DECLARES PARLIAMENT WILL STAND WITH MALAWIANS,BEGIN PROBES

Malawi Cables September 3, 2026
IMG_6457
  • Latest

VICE PRESIDENT ANSAH HOSTS AFRICAN BEAUTY QUEENS, CHAMPIONS REGIONAL CULTURAL COOPERATION

Malawi Cables September 3, 2026
1000161257
  • Latest

POLICE IN KARONGA ARRESTED A CHINESE NATIONAL FOR OPERATING ONLINE BUSINESS WITHOUT LICENCE

Andy Ten September 2, 2026
Copyright © 2026 All rights reserved. | ReviewNews by AF themes.
%d