Skip to content

Malawi Cables Online

We Report the Future — the Only Trusted Source of News with a Difference

Primary Menu
  • Home
  • Latest
  • News
  • Breaking News
  • Religion
  • Economics
  • Politics
  • Sports
  • Home
  • Blog
  • Home
  • Latest
  • “Munagula Teargas wambiri Kuposa chimanga”- Njawala Asambwadza MCP
  • Latest
  • Politics

“Munagula Teargas wambiri Kuposa chimanga”- Njawala Asambwadza MCP

Malawi Cables May 15, 2026 (Last updated: May 15, 2026)
IMG_3648

Mneneri wa chipani cha UTM Felix Njawala chipani cha MCP chinali ndi mwayi okonza magwiridwe a ntchito za a polisi mu zaka zisanu zomwe imalamulira.

Njawala walankhula izi pomwe ena otsatira chipanichi akudandaula ndi momwe apolisi agwirira ntchito yawo dzulo pomwe anathira utsi okhetsa msozi otsatira chipanichi.

Iwo akuti MCP inakanika kusintha momwe nthambi ya polisi imagwirira ntchito zake ndipo zimakanika kusiyanitsa polisi ndi chipani.

Njawala wati, “Munagula teargas wambiri kuposa chimanga cholinga muzitithila pazinthu zopanda pake. Munalanda ufulu wa anthu to demonstrate pomawathila teargas onse ofuna kupanga mademo.”

Iwo alemba izi pa tsamba lawo la mchezo kutsatira zomwe zinachitika dzulo.

Njawala wapitiliza kuti “Kuonjera pa teargas, munagulanso zikwanje nkumakhapa anthu police ndi army ili pompo osapanga kanthu.”

“Mudabwe kuti mmalo mokumverani chisoni anthu akusangalala. Muzigugude pa mtima panu ,muzilangize.” Anatero a Njawala.

About the Author

Malawi Cables

Administrator

Malawi Cables is a dedicated news platform committed to delivering timely, accurate, and credible coverage of events and stories from Malawi and beyond.We aim to inform, educate, and engage our readers through in-depth reporting, insightful analysis, and impactful storytelling that sets us apart.

Visit Website View All Posts

Like this:

Like Loading…

Related

Post navigation

Previous: Malawi Police Praised For Disciplining MCP Terrorists
Next: Mukanadekha Bwana Chakwera Osati Kukhala Yaviyavi-Gerald Kampanikiza

Related Stories

1000161687
  • Latest

EIGHT PEOPLE ARRESTED IN MANGOCHI IN CONNECTION TO VANDALISM OF CHILIPA POLICE UNIT AND COURT

Andy Ten September 3, 2026
IMG_6458
  • Latest

SPEAKER SAMEER SULEMAN DECLARES PARLIAMENT WILL STAND WITH MALAWIANS,BEGIN PROBES

Malawi Cables September 3, 2026
IMG_6457
  • Latest

VICE PRESIDENT ANSAH HOSTS AFRICAN BEAUTY QUEENS, CHAMPIONS REGIONAL CULTURAL COOPERATION

Malawi Cables September 3, 2026

Recent Posts

  • EIGHT PEOPLE ARRESTED IN MANGOCHI IN CONNECTION TO VANDALISM OF CHILIPA POLICE UNIT AND COURT
  • SPEAKER SAMEER SULEMAN DECLARES PARLIAMENT WILL STAND WITH MALAWIANS,BEGIN PROBES
  • VICE PRESIDENT ANSAH HOSTS AFRICAN BEAUTY QUEENS, CHAMPIONS REGIONAL CULTURAL COOPERATION
  • POLICE IN KARONGA ARRESTED A CHINESE NATIONAL FOR OPERATING ONLINE BUSINESS WITHOUT LICENCE
  • Mcdonald Mtetemera Appointed As Mighty Wanderers Acting Head Coach

Recent Comments

No comments to show.

Archives

  • September 2026
  • August 2026
  • July 2026
  • June 2026
  • May 2026
  • April 2026
  • March 2026
  • February 2026
  • January 2026
  • December 2025

Categories

  • Breaking News
  • Economics
  • Home
  • Latest
  • News
  • Politics
  • Religion
  • Sports

You May Have Missed

1000161687
  • Latest

EIGHT PEOPLE ARRESTED IN MANGOCHI IN CONNECTION TO VANDALISM OF CHILIPA POLICE UNIT AND COURT

Andy Ten September 3, 2026
IMG_6458
  • Latest

SPEAKER SAMEER SULEMAN DECLARES PARLIAMENT WILL STAND WITH MALAWIANS,BEGIN PROBES

Malawi Cables September 3, 2026
IMG_6457
  • Latest

VICE PRESIDENT ANSAH HOSTS AFRICAN BEAUTY QUEENS, CHAMPIONS REGIONAL CULTURAL COOPERATION

Malawi Cables September 3, 2026
1000161257
  • Latest

POLICE IN KARONGA ARRESTED A CHINESE NATIONAL FOR OPERATING ONLINE BUSINESS WITHOUT LICENCE

Andy Ten September 2, 2026
Copyright © 2026 All rights reserved. | ReviewNews by AF themes.
%d