Skip to content

Malawi Cables Online

We Report the Future — the Only Trusted Source of News with a Difference

Primary Menu
  • Home
  • Latest
  • News
  • Breaking News
  • Religion
  • Economics
  • Politics
  • Sports
  • Home
  • Blog
  • Home
  • Latest
  • MV Chambo Sitima ya Pa Madzi Ya Ku Mozambique Yapsa Itayaka Moto Pa Nyanja ya Malawi Mbali ya Tanzania
  • Latest

MV Chambo Sitima ya Pa Madzi Ya Ku Mozambique Yapsa Itayaka Moto Pa Nyanja ya Malawi Mbali ya Tanzania

Andy Ten October 11, 2026 (Last updated: October 11, 2026)

Sitima ya MV chambo ya dziko la Mozambique koma imayenda panyanja ya Malawi yapsa mdziko la Tanzania.

Pali nkhawa yoti anthu ambiri amwalira ndipo ena avulala pomwe sitimayi yayaka moto pakati pa nyanja pomwe imachokera ku doko la Mbamba Bay m’dziko la Tanzania, kupita ku Mozambique.

Sitimayi yapsera mdera lotchedwa Mbamba bay ku mbali ya Tanzania komwe Lake Malawi imatchedwa Ziwa Nyasa (Lake Nyasa) ndipo kumbali ya Mozambique amaitchula kuti
Lago Niassa (Lake Nyasa).

Malingana ndi malipoti sitimayi inanyamula madilamu 30 a petulo ndipo chiwerengelo cha anthu omwe amwalira komanso kuvulala sichikudziwika padakali pano.

Malipoti malipoti ena akuti moto-wo unayamba pomwe munthu wina amasuta fodya pafupi ndi zigubu (madilamu) zambiri za mafuta agalimoto, zomwe sitima-yo inanyamula.

ndipo anthu ambiri ataya miyoyo yawo kamba koti maboti amene anathamangira kokapulumutsa anthu pangozi-yi, anali ang’onoang’ono omwe analibe kuthekera konyamula chiwelengero chochuluka pakamodzi.

MV Chambo yakhala ikuyendanso pa Lake Malawi kuthandizira ntchito za maulendo apa nyanja m’dziko lino.

About the Author

Andy Ten

Editor

Journalist from Mangochi former student and University of Malawi, The Polytechnic

View All Posts

Like this:

Like Loading…

Related

Post navigation

Previous: TWO MEN ARRESTED IN MZUZU IN CONNECTION WITH A MURDER OF FOUR YEARS OLD GIRL

Related Stories

1000121313
  • Latest

TWO MEN ARRESTED IN MZUZU IN CONNECTION WITH A MURDER OF FOUR YEARS OLD GIRL

Andy Ten October 11, 2026
1000120578
  • Latest

APOLISI KU NTCHISI AMANGA MAYI WINA KAAMBA KOPHA MWANA WAKE WONGOBADWA KUMENE

Andy Ten October 10, 2026
1000120069
  • Latest

SCORCHERS YADYA MWA ZIMBABWE 2 KWA DUU

Andy Ten October 9, 2026

Recent Posts

  • MV Chambo Sitima ya Pa Madzi Ya Ku Mozambique Yapsa Itayaka Moto Pa Nyanja ya Malawi Mbali ya Tanzania
  • TWO MEN ARRESTED IN MZUZU IN CONNECTION WITH A MURDER OF FOUR YEARS OLD GIRL
  • APOLISI KU NTCHISI AMANGA MAYI WINA KAAMBA KOPHA MWANA WAKE WONGOBADWA KUMENE
  • SCORCHERS YADYA MWA ZIMBABWE 2 KWA DUU
  • AKASEWEDZE JELE ZAKA KHUMI KOMANSO ZISANU KAAMBA KOZEMBETSA MWANA KUTI AMUGULITSE

Recent Comments

No comments to show.

Archives

  • October 2026
  • September 2026
  • August 2026
  • July 2026
  • June 2026
  • May 2026
  • April 2026
  • March 2026
  • February 2026
  • January 2026
  • December 2025

Categories

  • Breaking News
  • Economics
  • Home
  • Latest
  • News
  • Politics
  • Religion
  • Sports

You May Have Missed

1000121290
  • Latest

MV Chambo Sitima ya Pa Madzi Ya Ku Mozambique Yapsa Itayaka Moto Pa Nyanja ya Malawi Mbali ya Tanzania

Andy Ten October 11, 2026
1000121313
  • Latest

TWO MEN ARRESTED IN MZUZU IN CONNECTION WITH A MURDER OF FOUR YEARS OLD GIRL

Andy Ten October 11, 2026
1000120578
  • Latest

APOLISI KU NTCHISI AMANGA MAYI WINA KAAMBA KOPHA MWANA WAKE WONGOBADWA KUMENE

Andy Ten October 10, 2026
1000120069
  • Latest

SCORCHERS YADYA MWA ZIMBABWE 2 KWA DUU

Andy Ten October 9, 2026
Copyright © 2026 All rights reserved. | ReviewNews by AF themes.
%d