If I were Richard Chimwendo, I would be knocking on Dan Lu’s door, ndalama abweze, nyimbo ija ndi trash, no passion, energy and creativity has been put into the song, munthuyi wangoyimba kuti athane nazo.
You see, what I noticed, artist aliyense amakhala ndi nyimbo imodzi yandale. Lucius analephera kufufuta Yellow, anayimbako ya UTM ndi MCP koma zero.
Mkasa nde wayimba, koma sadzafufuta mose wa lero, Dan Lu olo atatani sadzafufuta “lodzani zanu,” and “mumumva kuwawa” ya Chilima will remain the best hit of my uncle.
Last month nkasa anayimba ya MCP, ili kuti? Iyiyi ya Dan Lu singakwane 2 days akuyimvera, dead on arrival. Uyuyu abweze ndalama, wangodya za ulele, ndipo musamale, atha kukayimba “lodzani zanu” Ku Msonkhano wa MCP.
500 million mukanawapatsa anyamata a media a MCP wa miyoyo ikanasintha, nthawi yatha, boma lagwa ili, mukutenganso ndalama kupereka kwa anthu a opposition anyamata akutuwa, mwatani?