Skip to content

Malawi Cables Online

We Report the Future — the Only Trusted Source of News with a Difference

Primary Menu
  • Home
  • Latest
  • News
  • Breaking News
  • Religion
  • Economics
  • Politics
  • Sports
  • Home
  • Blog
  • Home
  • Latest
  • ANTHU OKWIYA AWONONGA MA OFESI A POLISI NDI KHOTI KU CHILIPA M’BOMA LA MANGOCHI
  • Latest

ANTHU OKWIYA AWONONGA MA OFESI A POLISI NDI KHOTI KU CHILIPA M’BOMA LA MANGOCHI

Andy Ten August 26, 2026 (Last updated: August 26, 2026)

Anthu okwiya ku Chilipa m’boma la Mangochi awononga ma ofesi a Polisi ndi a Khoti kuderali posatila kusamvana komwe kunabuka pakayendesedwe ka mlandu wakusowa kwa mwana wina m’derali.

Amina Tepani Daudi wofalitsa nkhani za a Polisi m’bomali watsimikiza kuti nkhaniyi yachitika pa 25 August 2026 makolo ndi achibale amwana wosowayu atakhumudwa ndi kusakhutila ndi momwe nkhaniyi ikuyendera.

“Chinachitika ndi chakuti munthu yemwe akuganizilidwa kuti akukhuzidwa ndi kusowa kwa mwanayo amumasula ku Polisi ya Mangochi. Apa anthuwo anamemeza anzawo ndikuswa madzenela 8 ndi Chitseko pa Polisi ndi madzenela anayi pa Khothi ya Chilipa,” Watero Daudi.

Daudi wati a Polisi akhazikitsa kafukufuku kuti apeze ndi kumanga anthu amene achita izi.

Izi zachitika patangotha chaka chimodzi anthu enanso atawononga Polisi ya Katema yomwe ndiyoyandikana ndi Polisi ya Chilipa.

About the Author

Andy Ten

Editor

Journalist from Mangochi former student and University of Malawi, The Polytechnic

View All Posts

Like this:

Like Loading…

Related

Post navigation

Previous: 35 YEARS OLD MAN DIED OF ELECTROCUTION IN MANGOCHI IN ATTEMPT TO REMOVE ELECTRICAL WIRE
Next: Applicants Cry Foul as Civil Service Commission Remains Silent on Parole Officer Recruitment

Related Stories

Screenshot
  • Economics
  • Home
  • Latest

Corrupt Health Workers, Broken Systems Cartel Behind Drug Shortages in Public Hospitals

Malawi Cables August 27, 2026
IMG_6255
  • Home
  • Latest

15 Months On, No Arrest, No Justice for the Murder of Malawi Cricket Coach Arjun Menon

Malawi Cables August 27, 2026
IMG_6247
  • Latest

Applicants Cry Foul as Civil Service Commission Remains Silent on Parole Officer Recruitment

Malawi Cables August 26, 2026

Recent Posts

  • Corrupt Health Workers, Broken Systems Cartel Behind Drug Shortages in Public Hospitals
  • 15 Months On, No Arrest, No Justice for the Murder of Malawi Cricket Coach Arjun Menon
  • Applicants Cry Foul as Civil Service Commission Remains Silent on Parole Officer Recruitment
  • ANTHU OKWIYA AWONONGA MA OFESI A POLISI NDI KHOTI KU CHILIPA M’BOMA LA MANGOCHI
  • 35 YEARS OLD MAN DIED OF ELECTROCUTION IN MANGOCHI IN ATTEMPT TO REMOVE ELECTRICAL WIRE

Recent Comments

No comments to show.

Archives

  • August 2026
  • July 2026
  • June 2026
  • May 2026
  • April 2026
  • March 2026
  • February 2026
  • January 2026
  • December 2025

Categories

  • Breaking News
  • Economics
  • Home
  • Latest
  • News
  • Politics
  • Religion
  • Sports

You May Have Missed

Screenshot
  • Economics
  • Home
  • Latest

Corrupt Health Workers, Broken Systems Cartel Behind Drug Shortages in Public Hospitals

Malawi Cables August 27, 2026
IMG_6255
  • Home
  • Latest

15 Months On, No Arrest, No Justice for the Murder of Malawi Cricket Coach Arjun Menon

Malawi Cables August 27, 2026
IMG_6247
  • Latest

Applicants Cry Foul as Civil Service Commission Remains Silent on Parole Officer Recruitment

Malawi Cables August 26, 2026
1000155630
  • Latest

ANTHU OKWIYA AWONONGA MA OFESI A POLISI NDI KHOTI KU CHILIPA M’BOMA LA MANGOCHI

Andy Ten August 26, 2026
Copyright © 2026 All rights reserved. | ReviewNews by AF themes.
%d