Mukhito Sapepesa: Tell Malawians To Vote For APM For Economic Recovery, Food Security

Newly appointed Democratic Progressive Party Secretary General Baba Peter Mukhito has told Malawians to vote for incoming President , Prof. Arthur Peter Mutharika and Democratic Progressive Party for economic development of the nation , food security and and continued infrastructure development.

He was speaking on Saturday at Katoto ground in Mzuzu where the Democratic Progressive Party leader Peter Mutharika and senior party officials were holding their first rally in Mzuzu , since the party appointed Mutharika as party’s bearer in 2025 elections .

In his remarks, Mukhito said : Ndaima kuti ndipereke report la chipani. Ma delegates akuno ku mpoto mogwirizana ndi ma delegates a pakati ku mmawa komanso ku mvuma anagwirizana kusankha Prof. Arthur Peter Mutharika ngati mtsogoleri wa chipani chathu cha Democratic Progressive . komanso ngati candidate pamasankho akubwera chaka cha mawa mu September.

A mukhito anapitiira Kuwauza a Malawi kuti Prof. Arthur Peter Mutharika anasankhidwa chifukwa ndiyekhayo angathe kuthetsa mavuto omwe abwera ndi chipani cha MCP, ndipo a Malawi akhale ndi chikhulupiriro kuti ndi chipani cha DPP chokha chomwe chingathetse mavuto amenewa.

Pamene Prof. Bingu wa Mutharika analowa m’boma 2004, anapeza vuto la njala ndipo patatha zaka ziwiri njala inagonjesedwa. Lero boma la MCP labweletsa njala yadzaoneni ndipo a Malawi akudya chitedze pomwe mu 2020 DPP isanachoke mmboma, anthu Amadya nsima kutaya, thumba la chimanga linali pa 5000 kwacha Koma pano liri pa 50,000 kwacha .

Amukhito anapitiliza kulingosola kuti mu 2014 mmene a Prof. Arthur Peter Mutharika amalowa mboma, anapeza chuma chitasokonekera ndi cashgate ndipo patatha zaka ziwiri akulamuka , Chuma chinayamba kuyenda bwino, ndalama zakunja zimapezeka Komanso Katundu otsika mtengo .

Iwo amema a Malawi Kuti akalembetse mwa unyinji ndicholinga choti mu 2025, azathe kubvotera DPP komanso Arthur Peter Mutharika pofuna kukozaso dziko la Malawi .

Malawi Cables

Malawi Cables is a dedicated news platform providing timely and accurate coverage of events and stories from Malawi and beyond. The website aims to inform and engage readers by delivering powerful analysis and reporting.

Related Posts

Leave a Reply

You Missed

National Intelligence Predicts Chakwera to Secure 17% Only in 2025 Elections

National Intelligence Predicts Chakwera to Secure 17% Only in 2025 Elections

Head of Intelligence Dokani Ngwira Working Illegally as Contract Expired on November 17, 2024

Head of Intelligence Dokani Ngwira Working Illegally as Contract Expired on November 17, 2024

MCP Thugs Attack National Intelligence Director and Assistant at Airport Demanding Their Payment For Disrupted Demos

MCP Thugs Attack National Intelligence Director and Assistant at Airport Demanding Their Payment For Disrupted Demos

Mwenifumbo promises new Mining Act, decentralizing MDF, Police recruitments and federalism

Mwenifumbo promises new Mining Act, decentralizing MDF, Police recruitments and federalism

BOUGHT, RIGGED, OR EARNED? KABAMBE’S PATH TO UTM’S PRESIDENCY

BOUGHT, RIGGED, OR EARNED? KABAMBE’S PATH TO UTM’S PRESIDENCY

Former Presidents APM,JB Muluzi Condems MCP Sponsored Thugs On Demostrators

Former Presidents APM,JB Muluzi Condems MCP Sponsored Thugs On Demostrators