Nkhani ili pamudzi pano ndiyakuti ku bomako anapangana kuti atibere K1 trillion ife Amalawi m’dzina la kugula mafuta.
Anapanga kakampani kawo kabodzabodza ndikukatsekula akaunti ku Banki, ali ndalama zizidutsira kumeneko. Nkhanga zaona.
N’chifukwa chake lero manyuzipepala akulu-akulu onse alemba za nkhaniyi, yomwe woyamba kulemba anali a The Investigator magazine. Umbava wopanda nawo manyazi.