Kodi mwavutika ndi kukwera kwa zinthu? Kumbukilani kuti mphamvu ndi chida chothetsela mavuto ndi voti yanu.
Kulembetsa mu kaundula wa zisankho kuyambika Lolemba pa 21 October, 2024.
Ma boma omwe ali mu gawo loyambilira ali motere:
Chigawo cha Kumpoto: Chitipa, Karonga, Karonga Town, Mzuzu City.
Chigawo Cha Pakati: Nkhotakota, Ntchisi, Salima, Dedza.
Chigawo cha kumwela: Balaka, Machinga, Chiradzulu, Neno, Phalombe, and Mulanje.