Skip to content

Malawi Cables Online

We Report the Future — the Only Trusted Source of News with a Difference

Primary Menu
  • Home
  • Latest
  • News
  • Breaking News
  • Religion
  • Economics
  • Politics
  • Sports
  • Home
  • Latest
  • RBM YATI DZIKO LINO LATSALA NDI NDALAMA ZAKUNJA (FOREX KWA DZIKO LINO ZOKWANILA MIYEZI IWIRI NDI MASIKU 12
  • Latest

RBM YATI DZIKO LINO LATSALA NDI NDALAMA ZAKUNJA (FOREX KWA DZIKO LINO ZOKWANILA MIYEZI IWIRI NDI MASIKU 12

Andy Ten November 24, 2026 (Last updated: November 24, 2026)

Bank yaikulu ya Reserve yatulutsa lipoti limene likuonetsa kuti dziko lino latsala ndi ndalama zakunja zomwe ndizosafikila pa mlingo woyenela wa miyezi itatu pamene zikuonetsa kuti dziko lino latsala ndi ndalama zokwana miyezi iwiri ndi masiku khumi ndi awiri.

Lipoti la Banki yayikulu m’dziko muno ya Reserve yati ndalama zakunja zomwe dziko lino lili nazo padakali pano zatsika kudutsa mlingo oyenera.

Malingana ndi lipoti la RBM yi dziko lino lili ndi ndalama zochepera $600 million (pafupifupi K1 trillion) zomwe ndizongokwanira miyezi iwiri ndi masiku khumi ndi awiri (12) kugulira katundu kuchokera m’mayiko a kunja.

Komabe, lipotili lati dziko lino lili ndi ndalama zoposa $523.9 million zomwe zinalipo mu nthawi ngati yomweyi chaka chatha.

Zomwe lipotili latulusa sikusiyana mlingo oyenera omwe mayiko amalimbikitsidwa kukhala nawo umene ndikukhala ndi ndalama zakunja zokwanira miyezi itatu.

Mulipotili zawonetsanso kuti dziko lino limaononga ndalama pafupifupi $3 billion (zomwe ndi pafupifupi K5.2 trillion) kugula katundu kunja kwa dziko lino.

Izi zikudza pamene dziko lino likudutsa mmavuto akulu akutsowa kwa mafuta agalimoto ndi zinthu zina zofunikila pa moyo kaamba ka kusowa kwa ndalama zakunjazi (forex).

About the Author

Andy Ten

Editor

Journalist from Mangochi former student and University of Malawi, The Polytechnic

View All Posts

Like this:

Like Loading…

Related

Post navigation

Previous: MBS FINES SEVERAL SHOPS IN LILONGWE FOR POSSESSING EXPIRED PRODUCTS AND POOR LABELING AND STORAGE
Next: 41-YEAR-OLD MAN ARRESTED IN LILONGWE FOR HAVING SEXUAL INTERCOURSE WITH A 16-YEAR-OLD GIRL

Related Stories

1795526464486
  • Latest

41-YEAR-OLD MAN ARRESTED IN LILONGWE FOR HAVING SEXUAL INTERCOURSE WITH A 16-YEAR-OLD GIRL

Andy Ten November 24, 2026
1795448174643
  • Latest

MBS FINES SEVERAL SHOPS IN LILONGWE FOR POSSESSING EXPIRED PRODUCTS AND POOR LABELING AND STORAGE

Andy Ten November 23, 2026
1795438771224
  • Latest

54-YEAR-OLD MAN SENTENCED TO 40 YEARS IMPRISONMENT WITH HARD LABOUR FOR HAVING SEX WITH HIS 16-YEAR-OLD DAUGHTER IN LILONGWE DISTRICT

Andy Ten November 23, 2026

Recent Posts

  • 41-YEAR-OLD MAN ARRESTED IN LILONGWE FOR HAVING SEXUAL INTERCOURSE WITH A 16-YEAR-OLD GIRL
  • RBM YATI DZIKO LINO LATSALA NDI NDALAMA ZAKUNJA (FOREX KWA DZIKO LINO ZOKWANILA MIYEZI IWIRI NDI MASIKU 12
  • MBS FINES SEVERAL SHOPS IN LILONGWE FOR POSSESSING EXPIRED PRODUCTS AND POOR LABELING AND STORAGE
  • 54-YEAR-OLD MAN SENTENCED TO 40 YEARS IMPRISONMENT WITH HARD LABOUR FOR HAVING SEX WITH HIS 16-YEAR-OLD DAUGHTER IN LILONGWE DISTRICT
  • 16 PEOPLE INJURED AS 478 PEOPLE HAVE LEFT DESPERATE FOLLOWING HEAVY RAINS AND STRONG WINDS IN MACHINGA DISTRICT

Categories

  • Breaking News
  • Economics
  • Home
  • Latest
  • News
  • Politics
  • Religion
  • Sports

You May Have Missed

1795526464486
  • Latest

41-YEAR-OLD MAN ARRESTED IN LILONGWE FOR HAVING SEXUAL INTERCOURSE WITH A 16-YEAR-OLD GIRL

Andy Ten November 24, 2026
1000107193
  • Latest

RBM YATI DZIKO LINO LATSALA NDI NDALAMA ZAKUNJA (FOREX KWA DZIKO LINO ZOKWANILA MIYEZI IWIRI NDI MASIKU 12

Andy Ten November 24, 2026
1795448174643
  • Latest

MBS FINES SEVERAL SHOPS IN LILONGWE FOR POSSESSING EXPIRED PRODUCTS AND POOR LABELING AND STORAGE

Andy Ten November 23, 2026
1795438771224
  • Latest

54-YEAR-OLD MAN SENTENCED TO 40 YEARS IMPRISONMENT WITH HARD LABOUR FOR HAVING SEX WITH HIS 16-YEAR-OLD DAUGHTER IN LILONGWE DISTRICT

Andy Ten November 23, 2026
Copyright © 2026 All rights reserved. | ReviewNews by AF themes.
%d